Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

  1. Home   »  
  2. Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

 

ZAMBIRI zogona m’kholamo,
Zosungika bwino ’mo;
Koma imodzi inasokeradi,
Nitayika m’thengomo
Kutali kuphiri loopsalo,
Kutali ndi mbusa wakeyo.

Ambuye, muli nazo zambirizi,
Kodi sizifikirazi?
Koma Mbusa nanena, “Yangayo
Yatayika naneyo;
Ngakhale njira njoopsadi,
Ndilinga kuphiri kuipezanso.”

Koma zina sizinadziŵa ayi,
Makwaŵa ’napyola ’Ye,
Ndi mdima woopsa wa usikuwo
Ambuye nailonda yake.
Anamva kulira kutaliko,
Naipeza yofoka, yakufayo.

Ambuye, wakuti ndi mwaziwo
Panjira ponsepo?
“Ndaukhetsa potsata iwetu,
Kukubweza ku kholalo.”
Ndi m’manja mwalaswa bwanjimo?
“Ndalaswa ndi minga pofuna iwe.”

Ndi ponse paphiri ndi padambopo
Ndi makwaŵa, indetu,
Kunakwera kupfuula Kumwambako,
“Kondwani, ndaipeza yanga!”
Nd’ angelo a Mlungu nabwezanso,
“Kondwani, Ambuye ’napeza yawo.”

Post navigation

Previous: Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,
Next: Hymn 181 PANALITU wakudwala

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 362 MUKHALE ndine, dzuŵalo laloŵa,
  • Hymn 588 Mlungu, Inutu,
  • Hymn 179 Ndinachimwa poganiza
  • Hymn 571 Kwa ife lero anabadwa
  • Hymn 128 ANTHU m’maiko onse
  • Hymn 1306 Ndi ine ndasaukadi,
  • Hymn 19 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 1698 Chinkana dziko lonselo
  • Hymn 1843 Chigwa choopsacho cha imfa ndikachilowera,
  • Hymn 831 Mundikumbutse, ndikapanda tulo, za Kumwambako;
  • Hymn 39 MUNASIYATU dziko lanulo,
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee!
  • Hymn 529 Zili nazotu nkhwimba zirombozo,
  • Hymn 1520 Mbuye, Mawu anu
  • Hymn 1829 Mulungu ndiye Mbusa wanga, sindisowa konse;
  • Hymn 39 Poyang’ana ena ndi ndalamatu,
  • Hymn 243 Mtima wanga udzakondwera,
  • Hymn 1214 Mwamva Mzimu wakewo,
  • Hymn 309 ANA akumwamba ndife,
  • Hymn 552 Analira ndaniyo
  • Hymn 381 Chakudya changa chabwino
  • Hymn 138 SANGALATSA akusowa, masiku alikutha,
  • Hymn 398 Lero lino mwatipatsa
  • Hymn 1322 Ntchito zanga zonsezo
  • Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 241 MTENDERE uli m’mtima mwathumu,
  • Hymn 1682 Atha masiku aja ansoni,
  • Hymn 229 POYAMBAPO ndakondwadi.
  • Hymn 1588 Wandiwombola inetu
  • Hymn 480 TIANA ife tingofoka,
  • Hymn 461 ANA inu, myamikeni
  • Hymn 359 Tonse timyamiketu,
  • Hymn 1432 Lero lino m’bale wanga,
  • Hymn 1470 Chikondi cha Mbuyathu
  • Hymn 1655 Mbuye Yesu,
  • Hymn 882 Kodi tikulema nazo
  • Hymn 223 Ndafoka, ndaipa,
  • Hymn 942 Kaamba chisomo cha Mbuyathu
  • Hymn 1416 Mbuye wanga ndilikumva,
  • Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 1115 M’munda wa Mbuyako
  • Hymn 438 TIYAMIKE Ambuye,
  • Hymn 170 YESU ponong’oneza, idzanitu;
  • Hymn 515 Kuphiri la ‘Zitona,
  • Hymn 1054 Ndilira mtima wakulapa
  • Hymn 152 AMBUYE wathu Yesu
  • Hymn 491 KWA Yesu ndi kwabwinoko,
  • Hymn 1634 Pakwitana Mbuye wanga
  • Hymn 1842 Pabande lolunjika andilondolera njira;
  • Hymn 814 Mutichiritse ifenso
  • Hymn 1397 Okwawa pansi inu,
  • Hymn 1101 Ngati mtima sumakonda
  • Hymn 1033 Mkristu gwiratu ntchito
  • Hymn 1200 Ambuye, m’imfamo
  • Hymn 366 MADZULO aja kalero
  • Hymn 1175 Sindinanyengedwa konse,
  • Hymn 964 Kodi simuona njira,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version