Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

  1. Home   »  
  2. Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

 

ANTHU m’maiko onse
Akhala mitundu;
Kapena m’dziko lino
Akhala anzathu;
Agona mwa zoipa,
Apulukiradi,

Ati, Mutilangize
Abale, bwerani.

Ngakhale alemera
Ndi chuma cha dziko,
Kodi akakondwera
Opanda Mulungu?
Kodi akhala mwaŵi
Otsata zawozo?
Iyai, awonongeka,
Apeza tsokalo.

Ndi ife akudziŵa
Chikondi cha Mlungu,
Kodi tidzaŵamana
Kuŵala kwa Kristu?
Chipulumutso! Inde,
Tichibukitsetu,
Kuti mitundu yonse
Ibwere kwa Yesu.

Akristu nyamulani
Maneno a Mulunguyo,
Ndi moyo lalikani
Pa dziko lonselo;
Ndi Yesu Mpulumutsi
Anatiferatu;
Adzabvomera onse;
Ndi Mwana wa Mlungu.

Post navigation

Previous: Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,
Next: Hymn 129 WODALA ndiye munthuyo,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 577 Adagona m’ndyeromo
  • Hymn 1051 Zin’sowa indedi
  • Hymn 266 Ukondwere moyo wanga,
  • Hymn 857 Mlungu amaunikira
  • Hymn 1373 Zamoyo zili m’thengo zonsezo,
  • Hymn 1663 Yesu Mbuye,
  • Hymn 749 Ndiye wodyetsa anthu omwewo,
  • Hymn 1484 Idzatu, idzatu
  • Hymn 371 Mulungu, anthu ‘fe
  • Hymn 206 YESU, mulikundipempha
  • Hymn 56 KU Mzinda wakuyerawo
  • Hymn 1633 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 1853 Etu ine, etu ine,
  • Hymn 341 PAKUPEMPHERATU
  • Hymn 584 Ndi angelo,
  • Hymn 98 YESU, Bwenzi la ochimwa,
  • Hymn 1202 Ndikhumba mtimawo
  • Hymn 892 Tilibe madalitso
  • Hymn 775 Mwa anthu onsewo
  • Hymn 1576 Khamulo liliko
  • Hymn 450 YESU, munditsogoza
  • Hymn 1831 M’mitsinje yamtendere mtima wanga aumwetsa;
  • Hymn 166 Yendani, Munthu Wachisoni,
  • Hymn 1666 Yesu, ndinutu chitsime
  • Hymn 1270 Ndayesa kudzikonzadi,
  • Hymn 715 Mwapatsa Mwana wanu, ndi
  • Hymn 1844 Pamaso pa adaniwo mwayala gome langa;
  • Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu
  • Hymn 628 E! chisomo chosaleka
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 114 NDIPO Eliya anati kwa Elisa:
  • Hymn 396 Mtitsogolere nthawi zonsezo;
  • Hymn 696 Ufumu wake udalitsa
  • Hymn 625 Chaka chino mutipatse
  • Hymn 681 Ankhondo a Mulungu ‘nu, yendani m’njiramo,
  • Hymn 573 Ambuye, tikutamandani
  • Hymn 916 Akondwerera anthu
  • Hymn 421 Ine ndine mlendo
  • Hymn 377 ANTCHITO a Mulungu ’nu
  • Hymn 183 Mlemekeze, bukitsani,
  • Hymn 1551 Mukhale m’kati mwathu,
  • Hymn 276 Dziko lonse mlambire
  • Hymn 1002 Haya! ‘Nzanga taonani Yoonekayo
  • Hymn 64 LERO Kristu anauka,
  • Hymn 1746 Mwachimwemwe, mwachisoni,
  • Hymn 1497 Simbani mobwereza,
  • Hymn 181 PANALITU wakudwala
  • Hymn 2 YEHOVA Mthandizi,
  • Hymn 405 POLENGA dzikoli
  • Hymn 936 Ukatha moyo wanga
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 1026 Inde nditaya chumacho,
  • Hymn 339 Tipempha,
  • Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.
  • Hymn 474 MPULUMUTSI, Mbusa wathu,
  • Hymn 597 Mlungu ali nane
  • Hymn 965 Mundiuze, aulendo,
  • Hymn 1648 Uko Kumwambako Mbuyangayo
  • Hymn 402 M’mtima mwangamu mlowemo,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version