Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu

  1. Home   »  
  2. Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu

Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu

 

MUMZINDA wa Mulungu
Moyera mulimo,
Ndiye amathu omwe
Olera ifewo;
Mitima yathu yomwe
Ikondwereratu,
Nikhala nawo Mzinda
Wakukongolawu.

Akondwerera anthu Zokoma zonsezi
Za midzi ya padziko
Lapansi lonseli;
Mtendere wake koma
Wa Mzinda wathuwo
Upambanditsa zonse
Zapansi pomwepo.

Ndi nkhondo ikaleka
Kwa Mlungu komweko,
Ndi ukapolo watha,
Udani wathanso;
Ndi zakuopsa zonse
Ndi zosauka zii!
Ndi mwayi wa kwa Mlungu
Udzoza mutu tho!

Post navigation

Previous: Hymn 328 KULIBE vuto
Next: Hymn 330 N’LOKOMA Dziko langa!

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 170 M’manda naukamo
  • Hymn 399 Tchimo lathu lonse, Yesu,
  • Hymn 972 Akristu limbikani,
  • Hymn 301 Mwanawankhosa
  • Hymn 381 MONGA zomera zonsezo
  • Hymn 449 Mzimu wakuipa
  • Hymn 1189 Ambuye Mulungu,
  • Hymn 31 Tamandani mbuye,
  • Hymn 1027 Tithawiranji ifetu?
  • Hymn 158 WOCHIMWA iwe, bweratu,
  • Hymn 1375 Ndi anamwali obvekedwa mbuu!
  • Hymn 206 Uzanitu abale,
  • Hymn 1607 Yesu, dzina ndi lomweli
  • Hymn 702 Mbuye wathu mutipatsa
  • Hymn 143 Lero lino Mbuye Yesu
  • Hymn 461 ANA inu, myamikeni
  • Hymn 821 Aleluya!
  • Hymn 519 Mverani, aimba anawo,
  • Hymn 975 Tiyeni, Akristu inu,
  • Hymn 351 Titi bwanji?
  • Hymn 376 Adzadalitsa ‘fe
  • Hymn 425 Ine ndine mlendo
  • Hymn 778 Mwini madalitso,
  • Hymn 1315 Ambuye ‘naitana ‘ne:
  • Hymn 1778 Angelo kwezani
  • Hymn 569 Tiimbe ndi kulalikira
  • Hymn 1460 Akuti anthu akumvera
  • Hymn 18 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 1662 Msandipitire, Yesu,
  • Hymn 72 YESU wakukoma mtima,
  • Hymn 55 Ambiri tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 1647 Kubweza inetu, kubweza inetu,
  • Hymn 74 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 96 Kodi mudzampembedza Mbuye
  • Hymn 905 Iwo asekera, iwo asekera,
  • Hymn 1842 Pabande lolunjika andilondolera njira;
  • Hymn 291 ULENDO wachikhrisitu ngosawutsa ndithu,
  • Hymn 1038 Limbikani nonse
  • Hymn 417 M’BWERE Mlungu Mbuye wathu,
  • Hymn 1698 Chinkana dziko lonselo
  • Hymn 1760 Amithenga a Mulungu
  • Hymn 799 Inu Mlungu kalelo
  • Hymn 580 Mwana wakuyera ‘Nu,
  • Hymn 138 Kumva ulikumva, ulikumva,
  • Hymn 166 NDICHITENJI kukapeza
  • Hymn 41 Tiyeni, tiyeni,
  • Hymn 1270 Ndayesa kudzikonzadi,
  • Hymn 612 Oyamika Mlungu mbwere,
  • Hymn 925 Kodi umadandaula:
  • Hymn 1484 Idzatu, idzatu
  • Hymn 763 Ndiponso m’manja chikhocho
  • Hymn 1233 Tsopano ndibukitsabe chikondi chanu chija
  • Hymn 1293 Chitsimecho cha mwaziwo
  • Hymn 1822 Lawani chikondano chake;
  • Hymn 1221 Bwenzi ndinamkomanayo,
  • Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!
  • Hymn 947 Akristu tonsefe, tikondwe m’Dzikoli
  • Hymn 1494 Mbiri yakalelomwe,
  • Hymn 1173 Sindinanyengedwa konse
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version