Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

  1. Home   »  
  2. Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,

 

ZAMBIRI zogona m’kholamo,
Zosungika bwino ’mo;
Koma imodzi inasokeradi,
Nitayika m’thengomo
Kutali kuphiri loopsalo,
Kutali ndi mbusa wakeyo.

Ambuye, muli nazo zambirizi,
Kodi sizifikirazi?
Koma Mbusa nanena, “Yangayo
Yatayika naneyo;
Ngakhale njira njoopsadi,
Ndilinga kuphiri kuipezanso.”

Koma zina sizinadziŵa ayi,
Makwaŵa ’napyola ’Ye,
Ndi mdima woopsa wa usikuwo
Ambuye nailonda yake.
Anamva kulira kutaliko,
Naipeza yofoka, yakufayo.

Ambuye, wakuti ndi mwaziwo
Panjira ponsepo?
“Ndaukhetsa potsata iwetu,
Kukubweza ku kholalo.”
Ndi m’manja mwalaswa bwanjimo?
“Ndalaswa ndi minga pofuna iwe.”

Ndi ponse paphiri ndi padambopo
Ndi makwaŵa, indetu,
Kunakwera kupfuula Kumwambako,
“Kondwani, ndaipeza yanga!”
Nd’ angelo a Mlungu nabwezanso,
“Kondwani, Ambuye ’napeza yawo.”

Post navigation

Previous: Hymn 177 ŴALIRA Yesu m’dziko linoli,
Next: Hymn 179 TUMPHATUMPHA moyo wanga,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1430 Ndipo pakulowa
  • Hymn 1670 Bwenzi ndiye wakufera,
  • Hymn 228 Ataya zoipa,
  • Hymn 80 KUDZA kwa Mbuye
  • Hymn 1516 Pakudera nkhawa ‘ne,
  • Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo
  • Hymn 856 Kuunika kuoneka
  • Hymn 1223 Ndidzaimba za Mulungu,
  • Hymn 751 Mongatu mawu anuwo,
  • Hymn 1317 Ambuye naitana ‘ne:
  • Hymn 982 Tiyeni Akristu,
  • Hymn 1003 Kanganani nkhondo yanu
  • Hymn 1078 Khalatu woyera
  • Hymn 1190 Aleluya, mlemekeze,
  • Hymn 1748 Ambuye tsopano lino,
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 480 TIANA ife tingofoka,
  • Hymn 1751 Mbuye ngwodalitsika,
  • Hymn 19 MULUNGU akhale nawo,
  • Hymn 655 Ndiphunzitseni, Mbuyetu,
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 144 AMENE adzavomereza ndithu,
  • Hymn 564 Ndi chifukwa atikonda,
  • Hymn 1183 Adalitsika, indetu,
  • Hymn 1184 Akondwerera nthawiyi
  • Hymn 1151 Pomulambira Yesu Mbuyanga,
  • Hymn 1720 Padzanja lachifundolo
  • Hymn 473 Mzinda woyerawo!
  • Hymn 1182 Chikhulupiro chomwenso
  • Hymn 165 ATATE,’nu, atate ’nu,
  • Hymn 150 MIPINGO iyo idzatu,
  • Hymn 135 USANABADWE, Yeremiya,
  • Hymn 1549 Mtitsutse titachimwa
  • Hymn 1715 Kodi misozi itisowa,
  • Hymn 720 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 522 Akazi anadza
  • Hymn 286 Atate, tifika pamaso panu;
  • Hymn 251 NDIFUNA Yesuyo,
  • Hymn 616 Dziko lathu lonseli
  • Hymn 1116 Kwawo kwa Mbuyako
  • Hymn 312 Atate, mupatse zomwe tapemphazi,
  • Hymn 1181 Adalitsika munthuyo
  • Hymn 888 Polowa ndi Inu
  • Hymn 152 Inde, Yesu, mundikonda,
  • Hymn 182 YESU watidzera, watidzera,
  • Hymn 293 LIMBA mtima mbale wanga
  • Hymn 1143 Tikhale ndithu pomwepo;
  • Hymn 286 ZOVUTA zoopsya ndi zosaukazi
  • Hymn 364 Ali wokhululukira;
  • Hymn 1185 Imfa ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 1073 Mwa ine myatse moto wanu wakuyera mbuu,
  • Hymn 1414 Zonse zinathedwadi;
  • Hymn 109 MUTHIRE, Yesu, m’mtimanga
  • Hymn 26 “Ndakukonda ku imfa
  • Hymn 1775 Oonadi mtima,
  • Hymn 87 Aleluya, mwandigula,
  • Hymn 1309 Ndi inetu ndidziwedi
  • Hymn 1295 Ambuye, mwazi wanuwo
  • Hymn 92 KONDA dzinalo la Yesu,
  • Hymn 201 Ngati zakuipa zathu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version