Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

  1. Home   »  
  2. Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

 

M’MENE umauka m’maŵa,
Sunagwire ntchitozo,
Sunayambe kukayenda,
Ugwadire Mlunguyo.
Pena uli kusekera,
Pena nkhaŵa m’mtimamo,
Wachimwemwe, wachisoni,
Uza Yesu zonsezo.

Wakuchezacheza naye
Ukagwira ntchitozo;
Pakukumbukira Yesu,
Nkhaŵa zidzachokanso
Ndi zapansi zikafuna
Kukudzaza m’mtimamo,
Utsogole kopemphera,
Uza Yesu zonsezo.

Ndi m’kutero udzadziŵa
Chifuniro chakecho; Iye adzakuthandiza
Uthangate enanso:
Ndi ofoka ulimbitse,
Akulapa bwezatu;
Ndi za ntchito zake izi
Uza Yesu zonsezo.

Ndipo ngati ungolema,
Ulefuka m’dzulomo,
Ndi Satana akayesa
Kukukola m’mtimamo:
Wakufoka, wakuopa,
Penyetsetsa Iyeyo;
Udzakhazikika m’mtima
Pakumuza zonsezo.

Post navigation

Previous: Hymn 405 POLENGA dzikoli
Next: Hymn 407 ADZAPAMBANA Yesu ponse

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 705 Tikhaletu nawo, Mbuye,
  • Hymn 813 Wopulumutsa, Inunso
  • Hymn 1517 Lindionetsera ‘ne,
  • Hymn 1112 Masiku anga onse
  • Hymn 1508 Mundinyemere ‘ne
  • Hymn 144 Yesu, ndipemphera
  • Hymn 882 Kodi tikulema nazo
  • Hymn 445 Mlewe oipawo,
  • Hymn 269 NDILIRA ine kukayenda
  • Hymn 1012 Ndi zipatsozo,
  • Hymn 333 M’DZIKO lino tikhalamo
  • Hymn 1034 Mkristu, ulimbike
  • Hymn 175 Mlungu mverani, mphamvu patseni,
  • Hymn 469 NDIKONDA mbiri yomwe
  • Hymn 76 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 117 CHOLIMBITSA mtima ndi chonditsogolera;
  • Hymn 1591 Sizitha ntchito zangazo,
  • Hymn 1124 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 433 Zoipa ndi zabwino
  • Hymn 334 Tsugulani mtima wanu
  • Hymn 282 INU muli mehere,
  • Hymn 1241 Ati: Mwana, kumbukira
  • Hymn 1700 Ambuye Mwini moyo,
  • Hymn 182 YESU watidzera, watidzera,
  • Hymn 850 Pemphero, pemphero,
  • Hymn 478 Ndife ana, mutikonda,
  • Hymn 512 ‘Natipulumutsa
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 213 Mawu a Yesu ati: “Msangatu
  • Hymn 112 ELISA mneneri,
  • Hymn 1529 Mndithandize kukondana
  • Hymn 1651 Kwa Mulungu m’Mwambamo
  • Hymn 101 MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,
  • Hymn 1177 Ndidziwitsitsa Yesu ndi wanga,
  • Hymn 379 Anditsogolera m’njira
  • Hymn 1488 Musawalole mawuwo
  • Hymn 253 YESU ndinutu wanga m’njira zonse,
  • Hymn 1833 Podwala ine pobvutidwa Andisamalira;
  • Hymn 1417 Atate ‘nu, atate ‘nu,
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 97 Maso ndi maso ndi Kristu,
  • Hymn 776 Tikondwereratu
  • Hymn 400 Dzuwa liwala, m’tulotu
  • Hymn 8 MITAMBO inu yakumwambako
  • Hymn 728 A! Yesu, ndapangana
  • Hymn 16 Chikhulupiriro chathu
  • Hymn 499 ‘Nafera Mbuye wanga
  • Hymn 16 MTIMA wanga lemekeza,
  • Hymn 527 Idzani mumtima mwanga,
  • Hymn 762 “Ndi thupi lopatsidwali
  • Hymn 812 Ndi ena sanamvera ‘yi,
  • Hymn 649 Inde, tikuyamikani, Atate, leroli,
  • Hymn 836 Kamoyo kanga katha lero lino,
  • Hymn 35 KODI mwaona chiyani,
  • Hymn 1584 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 1402 Mverani Iye ati: idzanitu;
  • Hymn 1365 Zozizwa za m’dziko,
  • Hymn 529 Zili nazotu nkhwimba zirombozo,
  • Hymn 972 Akristu limbikani,
  • Hymn 230 AMBUYANGA Yesu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version