Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 112 ELISA mneneri,

  1. Home   »  
  2. Hymn 112 ELISA mneneri,

Hymn 112 ELISA mneneri,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 112 ELISA mneneri,

 

ELISA mneneri,
Wachita zamphamvu;
Kuyandamitsa nkhwangwayo,
Pa Yolodani’po.

(M) Nkhwangwayo,
(O) Ndiyobwereka,
Nalira mnyamatayo;
Popeza ndiyobwereka,
Pa Yolodanipo.

Elisa mneneri,
Natenga kamtengo;
Naponya pamadzi paja,
Nkhwangwa niyandama.

Mulungu wamphamvu,
Natuma Mwana ‘ke;
Kuti atifere ife,
Kutipulumutsa.

Nanga ife lero,
Kodi takonzeka;
Kusiya machimo athu,
Kutsata Yesuyo?

Post navigation

Previous: Hymn 111 YAKOBO mwanatu wachinyengoyo;
Next: Hymn 113 KALERO anthu onse

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 40 KAMWANA Yesu ’nabadwa,
  • Hymn 162 PENYETSETSA Yesu,
  • Hymn 800 Yesu munadzukanso
  • Hymn 879 Zokoma etu nthawizi”
  • Hymn 310 Tafika kwa inu mutiunikire,
  • Hymn 1194 Padziko lapansi
  • Hymn 1637 Tisaleke kugwirabe
  • Hymn 1163 Tili ndi mtendere
  • Hymn 1452 Inu akutopawo,
  • Hymn 1187 M’mitima mwathu mwakhala mbee!
  • Hymn 134 Aleluya, Aleluya!
  • Hymn 1403 ‘Mvani liwu lomwe
  • Hymn 234 Kwa kutha kwa moyo,
  • Hymn 263 Mulungu wakwezekatu,
  • Hymn 332 Perekani mtima wanu,
  • Hymn 26 “Ndakukonda ku imfa
  • Hymn 433 Zoipa ndi zabwino
  • Hymn 1433 Lero lino ndi labwino;
  • Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu
  • Hymn 1542 Titamire nthawi zonse
  • Hymn 155 Pemphero ndiko kufuna
  • Hymn 1679 Tiyamike Dzina lake, Aleluya,
  • Hymn 1648 Uko Kumwambako Mbuyangayo
  • Hymn 482 Ndinu wakuyera,
  • Hymn 269 Atate ‘nu, amayi ‘nu, nonsenu,
  • Hymn 1539 Kudzoza kwa Kumwambako
  • Hymn 593 Yesu, munditsogoza
  • Hymn 1384 Mphamvu yake inalenga
  • Hymn 1407 Tula mtolo wako
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 1316 Ndabwera kwa Ambuyeyo:
  • Hymn 150 MIPINGO iyo idzatu,
  • Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,
  • Hymn 338 ’TATE wa Kumwambako,
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 1285 Yesu, n’kupatsani zonse,
  • Hymn 1364 Uzani zamphamvu,
  • Hymn 456 Tizikondana, tisekere
  • Hymn 25 “Akaleka amake
  • Hymn 1725 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 832 Zochimwa za usana uno mndikhululukire ‘ne;
  • Hymn 1590 Mtima ndimakondweramo,
  • Hymn 1624 Koma anthu onse omwe
  • Hymn 75 MBUYE, mutsaganetu
  • Hymn 1050 Ndafoka inetu,
  • Hymn 435 ANAKWATIRA kale
  • Hymn 1043 Mbiri yake ubukitse,
  • Hymn 234 IMFA ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 645 Kristu ndiye mwala wathu,
  • Hymn 530 Munaneneratu mawu a moyonso
  • Hymn 141 TAONANI pamtandapo,
  • Hymn 1269 Ndifoka ndi zoipazo,
  • Hymn 600 Mbuye Yesu, myandikire,
  • Hymn 216 NDISAUKA, ndinachimwa,
  • Hymn 965 Mundiuze, aulendo,
  • Hymn 618 ‘Dzani Mbuye msangatu,
  • Hymn 1759 Powalitsira omwe
  • Hymn 399 M’KHOLA mwa ng’ombe ku Betlehemu
  • Hymn 228 Ataya zoipa,
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version