Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 35 KODI mwaona chiyani,

  1. Home   »  
  2. Hymn 35 KODI mwaona chiyani,

Hymn 35 KODI mwaona chiyani,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 35 KODI mwaona chiyani,

 

KODI mwaona chiyani,
Anzeru a kummawa?
Nyenyezi’yo yaoneka,
Isonyeza njirayo.

Mtendere padziko lonse,
Mtendere padziko lonse;
Kwa anthu onse amene,
Alandira Yesuyo.

Nyenyeziyo pooneka,
Isonyeza chikondi;
Kuti Yesu wabadwadi,
Mu kholalo la ng’ombe.

Ndipo iye wolandira,
Ambuye wathu Yesu;
Akhalanso nawo zedi,
Moyowo wochuluka.

Post navigation

Previous: Hymn 34 AMITHENGA a Mulungu,
Next: Hymn 36 AMBUYE tsopano lino, monga mwa mawu anu aja,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 400 Dzuwa liwala, m’tulotu
  • Hymn 1555 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 295 Kubadwa kwa Yesu
  • Hymn 500 >AMEN, Amen, Amen.
  • Hymn 678 Ibukike mbiri yanu,
  • Hymn 899 ‘Tate wa Kumwambako,
  • Hymn 1229 Dzinalo la Yesu,
  • Hymn 737 Mommuno, Mbuye, tionanetu,
  • Hymn 777 Mulungu ali muno,
  • Hymn 495 Wonga Inu ndikhaledi,
  • Hymn 416 PALIBE wina Kumwamba,
  • Hymn 135 USANABADWE, Yeremiya,
  • Hymn 9 TAMANI Ambuye,
  • Hymn 1577 “Kwa Iye atikonda
  • Hymn 1462 Dzina la Yesu ndi lokoma,
  • Hymn 1135 Mulungu anditsogolera,
  • Hymn 1425 Apempha malo Ambuye;
  • Hymn 219 Mtenderewo wosanyenga
  • Hymn 1809 Yampatsa Nowa yemwe,
  • Hymn 224 Atero ndaniyo?
  • Hymn 1369 Paphiri paja papakulupo,
  • Hymn 132 Ganizansoni, ali pano,
  • Hymn 1666 Yesu, ndinutu chitsime
  • Hymn 1445 Tiyeni tonse, tinkeko
  • Hymn 1216 Ndatsatatsatabe
  • Hymn 771 Tsopano alandira
  • Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
  • Hymn 1834 Chisomo ndi zokoma zake sizileka konse;
  • Hymn 811 Wopulumutsa mudzetu;
  • Hymn 1705 Pa Iye padzapo
  • Hymn 453 Tiana ta Ambuye tili
  • Hymn 1205 Ndikonda chifukwa
  • Hymn 1725 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 446 Yesu alandira
  • Hymn 118 PANALI munthu amene,
  • Hymn 251 Kuli chimwemwe m’dzuwalo
  • Hymn 613 Dziko lonse nla Mulungu
  • Hymn 1437 Yesu ndi wokonda;
  • Hymn 1156 Imfa ndi manda sitiopa ‘yi,
  • Hymn 201 NDILINKUDZA kwa Ambuye,
  • Hymn 582 A! Mulungu,
  • Hymn 62 Tchimo lonse ligonjera
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 714 Dzuwa ndi mvula yonseyo
  • Hymn 1153 Mtendere uli m’mtima mwathumu,
  • Hymn 337 PADZIKO pano tikhalira M’moyo wosauka;
  • Hymn 929 Chikondano sichifera;
  • Hymn 1802 Mulungu anatuma,
  • Hymn 111 Nkhope yake ‘kabisika,
  • Hymn 343 Auke,
  • Hymn 328 KULIBE vuto
  • Hymn 872 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 343 ZOKOMA ndithu nthaŵizi
  • Hymn 993 Pakumalizidwa
  • Hymn 75 MBUYE, mutsaganetu
  • Hymn 82 Mlendo wa Kumwambayo
  • Hymn 129 WODALA ndiye munthuyo,
  • Hymn 51 PANTHAWI yakufa Ambuye,
  • Hymn 1643 Kufuna inetu, kufuna inetu,
  • Hymn 862 Tidza kwa Mulungu Inu, ndinu wa chifundo;

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version