Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,

  1. Home   »  
  2. Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,

Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,

 

TITAME Mlungu Wakumwamba,
Timwimbire nyimbo,
Kukoma kwake kwatipatsa
Zonse tili nazo.

(Timwimbire nyimbo,
Timwimbire nyimbo!
Kukoma kwake kwatipatsa
Zonse tili nazo)

Poyamba paja analenga
Zonse dziko muno,
Tsopano lomwe azisunga
Zonse zili moyo.

Tinasokera ngati nkhosa,
Moyo tinataya,
Tinakondwera ndi zoipa
Zonse tinatsata.

Komweko titasaukira,
Titafuna kufa,
Atate anatilondola
Naitana ife.

Tiyeni tizipita kwathu,
Tisasokerenso,
Tilape m’mtima kuti
tikakhale ndi Mulungu.

Post navigation

Previous: Hymn 23 TIIMBE nyimbo zotamanda
Next: Hymn 25 ANGELO amayimba,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 314 E, moto wanu woyera
  • Hymn 119 Tamverani anthu inu,
  • Hymn 129 Mudze kwa Yesu, musachedwe,
  • Hymn 468 NDIKONDWA kuti
  • Hymn 831 Mundikumbutse, ndikapanda tulo, za Kumwambako;
  • Hymn 567 M’nyumba zonse ponseponse
  • Hymn 22 MU ZONSE abale yamikani,
  • Hymn 797 Kwacha lero kwati mbee,
  • Hymn 1053 Mtimatu wopirira ndi
  • Hymn 644 M’wasunge, m’wayendetse
  • Hymn 841 Mukhale, mukhale,
  • Hymn 38 ANGELO ayimba,
  • Hymn 356 Tinafena m’nyanjamo,
  • Hymn 807 Mpulumutsi tikagona
  • Hymn 369 Lowani m’nyumba mwakemu
  • Hymn 275 Mlungu akuyang’aniredi,
  • Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,
  • Hymn 1458 Satana ndi unyolo
  • Hymn 1510 Mtume tsopanoli
  • Hymn 1167 Mulungu wanga,
  • Hymn 1636 Potuluka m’manda mwawo
  • Hymn 379 Anditsogolera m’njira
  • Hymn 380 Ndipyola kodi chikhwawa
  • Hymn 174 YESU wathu Mbuyeyo
  • Hymn 1671 Akhululukira iwe,
  • Hymn 1143 Tikhale ndithu pomwepo;
  • Hymn 1141 Pakulekana ifetu
  • Hymn 281 MBUYE, mwatiuza ’fe
  • Hymn 421 ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,
  • Hymn 52 Mbwere Mzimu, mbwere!
  • Hymn 327 Yesu salephera ‘yi.
  • Hymn 312 NDIMAYENDA paulendo
  • Hymn 485 Mukatiitana
  • Hymn 26 NDIKULEMEKEZA
  • Hymn 1445 Tiyeni tonse, tinkeko
  • Hymn 1417 Atate ‘nu, atate ‘nu,
  • Hymn 1481 Timsankhe Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 1339 Musaope pokumbuka
  • Hymn 302 Anasenza m’thupi mwake;
  • Hymn 436 YEHOVA Mlungu wathu,
  • Hymn 34 AMITHENGA a Mulungu,
  • Hymn 506 Ndikondwa kuti Yesu akonda,
  • Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,
  • Hymn 69 KONDWERANI dzuŵa lino,
  • Hymn 1047 Ambuye, chotsani zonse zomwezo
  • Hymn 340 Imvani,
  • Hymn 1579 Akhala mafumu
  • Hymn 381 Chakudya changa chabwino
  • Hymn 212 Onse am’Mwamba ali mowemo,
  • Hymn 477 Mpulumutsi, Mbusa wathu,
  • Hymn 178 Machimo anga ngambiri
  • Hymn 1465 Akulu inu m’bwere nonse,
  • Hymn 301 MBUYE, ndapangana
  • Hymn 769 Ndi kutsukidwa m’mwazimo
  • Hymn 883 Pokupempherani
  • Hymn 1678 Yesu nkana saoneka, Aleluya,
  • Hymn 41 MKATI mwa zovuta zathu
  • Hymn 948 Tiimbe mokondwa, misozi iume;
  • Hymn 1714 Tiyeni, dzalireni nane,
  • Hymn 182 YESU watidzera, watidzera,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version