Hymn 1786 Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1786 Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga Amva pemphero ndi kulira kwanga, Namatchereza khutu nditapfuula, Andithandiza, nandipulumutsa.