Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 276 MKRISTU, ulimbike

  1. Home   »  
  2. Hymn 276 MKRISTU, ulimbike

Hymn 276 MKRISTU, ulimbike

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 276 MKRISTU, ulimbike

 

MKRISTU, ulimbike
M’ntchito yakeyo;
Yesu anafera
Anthu akewo.

Mphamvu zathu zonse
Tionetsenso,
Kuti kudziŵike
Tili akewo.

Mtima wakufatsa
Amakondako;
Ndipo anthu onse
Angatengero.

Mapemphero athu
Tikakwezebe,
Dzina lake lomwe
Tiyamike ’fe.

Limbikani nonse
Mpaka imfayo.
Ndipo Mfumu yathu
Idzakondwatu.

Post navigation

Previous: Hymn 275 NTHAWI yathu yafikatu,
Next: Hymn 277 GWIRA zintchito zako,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 578 Falitsani mbiriyi,
  • Hymn 1120 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 749 Ndiye wodyetsa anthu omwewo,
  • Hymn 839 Adani sindiopa mukalipo;
  • Hymn 117 Atate wondipatsazo,
  • Hymn 72 Mayi watsogola ku Ulemerero,
  • Hymn 441 MBUYE, tikuthokozani,
  • Hymn 46 INALIPO nthawi,
  • Hymn 1102 Dziko lonse ndilitaya;
  • Hymn 1019 Tsata, tsata, nditsatadi Yesu;
  • Hymn 245 Ngakhale kuthengo
  • Hymn 26 NDIKULEMEKEZA
  • Hymn 464 AKAZI anadza kwa Yesu ndi anawo,
  • Hymn 681 Ankhondo a Mulungu ‘nu, yendani m’njiramo,
  • Hymn 464 Yesu atiuza tiyambemo,
  • Hymn 823 M’mwambamo nyenyezi
  • Hymn 1496 Mawu amveke bwino,
  • Hymn 551 Ndani kodi Munthuyo
  • Hymn 1806 Nowayo anatuma,
  • Hymn 549 Ndiye Mbuye, Mfumu yanga,
  • Hymn 342 BWENZI lathu ndiye Yesu,
  • Hymn 307 ABALE anga ine ndikupita,
  • Hymn 831 Mundikumbutse, ndikapanda tulo, za Kumwambako;
  • Hymn 175 A! MBUSA wathu amvatu
  • Hymn 351 Titi bwanji?
  • Hymn 956 Mbuye munditsogolere,
  • Hymn 1655 Mbuye Yesu,
  • Hymn 885 Mndimvetse chisoni
  • Hymn 853 Pa tsikuli, Mbuyanga ‘Nu,
  • Hymn 651 Ikhale ngati nyali
  • Hymn 1545 Mundilimbitse m’mtima
  • Hymn 1811 Tipulumuka mommo,
  • Hymn 820 Ndife ananu,
  • Hymn 1446 Inu nonse obvutidwa,
  • Hymn 1055 E, mtima watsopano ndi
  • Hello world!
  • Hymn 1233 Tsopano ndibukitsabe chikondi chanu chija
  • Hymn 1006 Yesu ati, “Ndidza msanga!”
  • Hymn 1012 Ndi zipatsozo,
  • Hymn 1780 Titame Mlungu Wakumwamba,
  • Hymn 81 Imva mawu akewo,
  • Hymn 81 MBUYE Yesu adzabwera,
  • Hymn 1558 Wosangalatsa, ine ndikalira
  • Hymn 816 Mdima wafika,
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 1016 Mbuye, mwatiuza ‘fe
  • Hymn 294 Yesu anali khanda
  • Hymn 1064 Moyowo
  • Hymn 1782 Poyamba paja analenga
  • Hymn 378 KWEZANI mitu yanuyo,
  • Hymn 1819 Pokondwa ndi poona bvuto
  • Hymn 415 Tidzalandirabe komwe
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 302 NDIDZE pafupi pa
  • Hymn 491 N’takafika kwanu
  • Hymn 497 TILIKUIMBA nyimbo yomweyi,
  • Hymn 748 Ndiye wa moyo wonse Mwiniyo,
  • Hymn 1826 Amadyetsa Iye mbalame zam’mwamba,
  • Hymn 424 MTIDZUTSE, Mbuyetu,
  • Hymn 1569 Mtima wodetsa mukonzere,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version