Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 448 CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,

  1. Home   »  
  2. Hymn 448 CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,

Hymn 448 CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 448 CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,

 

CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,
Tim’lambire Mbuye;
Tikweze nyimbo yakukondwa kuli ‘Ye,
Tim’gwadiretu.

Dzinja lokondweretsa lafikanso, litapumatu,
Tim’lambire Mbuye;
Mvula igundanso,
Mulungu wotikonda ‘fe,
Tim’gwadiretu.

Dziko lonse lili kukondwa, mlengalenga, mpheponso,
Tim’lambire Mbuye;
Zapansi pano zonse zim’tamandire,
Mulungu wathuyo,
Tim’gwadiretu.

Maluwa abwino aphuka m’mapiri, ndi m’madambomo,
Tim’lambire Mbuye;
Masamba ‘awisi, aang’ono agwedezekanso,
Tim’gwadiretu.

Zanu zapansi n’zokoma
Mbuye; tikondwera ‘fe,
Tim’lambire Mbuye;
Koma kwanu Kumwamba komwe kwapambanatu,
Tim’gwadiretu.

Nafenso tidzauka kwa
‘kufa ngati maluwawo,
Tim’lambire Mbuye;
Oyera mtima adzavala mbuu! pakudza Khrisituyo,
Tim’gwadiretu.

Tidzakhala naye nthawi zonse, ndi kuyimbako,
Tim’lambire Mbuye;
Kumene moyo wa anthu okhululukidwa uli wokomatu,
Tim’gwadiretu.
Aleluya, Amen!

Post navigation

Previous: Hymn 447 OYAMIKA Mlungu m’bwere,
Next: Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 305 M’mwazi wake tisambamo;
  • Hymn 348 Aitana,
  • Hymn 1751 Mbuye ngwodalitsika,
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,
  • Hymn 1736 “Senzani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 239 Akumwambawo
  • Hymn 396 PETURO ’nafunsa Hananiya:
  • Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?
  • Hymn 1304 Ndi ine sizitheka ‘yi
  • Hymn 1064 Moyowo
  • Hymn 1693 Koma masauko ake Aleluya
  • Hymn 1340 Perekani mtima wanu
  • Hymn 226 Nditama mwaziwo!
  • Hymn 1159 Mwalembedwa mukalata
  • Hymn 742 Tikadya phando zaka zonsezi,
  • Hymn 964 Kodi simuona njira,
  • Hymn 47 YESU panjirayo,
  • Hymn 360 KRISTU wakuyeratu,
  • Hymn 484 YESU ndiye Mbusa,
  • Hymn 1386 Ndi chifundo atipenya
  • Hymn 1514 Dzinthu zakumundazo
  • Hymn 182 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 1745 Yesu aitana ife:
  • Hymn 210 PEREKANI mtima wanu,
  • Hymn 9 TAMANI Ambuye,
  • Hymn 1096 Tifuna Inu, Mbuye,
  • Hymn 709 Munthu aganize
  • Hymn 876 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 1487 Bvumbulutsa zonse zako
  • Hymn 1740 Yesu, ndi chifundo chanu
  • Hymn 105 IDZANI, Mzimu Inu,
  • Hymn 659 Anthu ali m’mdima akuitanitsa
  • Hymn 1173 Sindinanyengedwa konse
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 215 Choka, choka,
  • Hymn 1507 Ndikampempha anditenge,
  • Hymn 842 Tipempha kuti Mpingo wanu
  • Hymn 1552 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 803 Mulungu wanga, Dzuwatu
  • Hymn 44 Mlungu dalitsani Malawi,
  • Hymn 40 KAMWANA Yesu ’nabadwa,
  • Hymn 1185 Imfa ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 298 IFE tazingidwa ndi zinthu zoopsa,
  • Hymn 460 E! ang’ono ndifetu,
  • Hymn 82 YANG’ANANI, anthu onse,
  • Hymn 249 MBUYANGA Yesu, mundigwire
  • Hymn 1031 Gwira zintchito zako,
  • Hymn 570 Ndikhulupirira Yesu
  • Hymn 309 Mwa Mzimu mulowe mumitima yathu,
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 264 Bvinabvina moyo wanga,
  • Hymn 938 A! Yesu Bwenzi langa
  • Hymn 902 Ndikondwa kuganizabe
  • Hymn 1615 Anakonda,
  • Hymn 819 Lero tigone,
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 99 Tsopano ndimwona Iye
  • Hymn 161 Tibwera ndi tianato
  • Hymn 1292 Wolapa mtima simunyozadi,
  • Hymn 100 MUBWERE Mzimu Wakuyera,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version