Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 9 TAMANI Ambuye,

  1. Home   »  
  2. Hymn 9 TAMANI Ambuye,

Hymn 9 TAMANI Ambuye,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 9 TAMANI Ambuye,

 

TAMANI Ambuye,
Wamphamvu ndi Iye;
Akhala m’ulemu,
Kumwamba komweko.
Chikopa cholimba,
Ndi kothaŵiranso;
Kwa anthu akewo,
Kotero ndi Mlungu.

Uzani zamphamvu,
Imbani chisomo;
Za Mwini ulemu,
Ambuye wathuyo.
Poomba chimphepo
Mvulanso ndi bingu;
Padziko, pathambo,
Akhala ponsepo.

Zozizwa zam’dziko,
Za M’mwamba zonsezi;
Mulungu wamphamvu,
Munalenga zonse;
Muyendetsa mwezi,
Nyenyezi ndi dzuŵa;
Zolengedwa zonse,
Zimvera Ambuye.

Sitiha ifedi,
Kukamba zokoma;
Za Inu Mulungu,
Wolera anthuwa.
Zifika ndi mphepo,
Ndi mvula ndi dzuŵa;
Zigwera ponsepo,
Pa anthu onsewa.

Wamphamvu yosatha,
Chikondichangwiro;
Angelo akonda,
Kutama Mulungu.
Ndiponso ifetu,
Ana ‘nu tonse ‘fe;
Tiimba nyimboyi,
Yotama Ambuye.

Post navigation

Previous: Hymn 8 MITAMBO inu yakumwambako
Next: Hymn 10 TSOPANO linoli,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 834 Tiyamike Mlungu wotipatsa zachifundozi,
  • Hymn 1513 M’Bukuli ine ndi
  • Hymn 392 ANU Mbuye ndifetu!
  • Hymn 323 >APITA anzathu dzuŵa lino
  • Hymn 104 M’mene ntchito yathatu,
  • Hymn 1150 Pamtanda Mbuyanga ‘nafera,
  • Hymn 720 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 140 NDINAMIRA m’machimo, wosaonekanso,
  • Hymn 1659 Ndiye mtsamiro
  • Hymn 79 Mlendo ali pakhomo,
  • Hymn 421 Ine ndine mlendo
  • Hymn 453 A! MULUNGU
  • Hymn 717 Ambuye zathu zonsezi
  • Hymn 1529 Mndithandize kukondana
  • Hymn 756 Sindili woyenera ‘ne,
  • Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo
  • Hymn 875 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 131 MAWU a Mulungu awa,
  • Hymn 1735 “Sezani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 1633 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 37 YESU analikhanda
  • Hymn 318 TINALI ambiri ife,
  • Hymn 367 MPULUMUTSI, tikagona
  • Hymn 285 Ndipempha, Ambuye,
  • Hymn 1171 Mulungu wanga
  • Hymn 763 Ndiponso m’manja chikhocho
  • Hymn 815 Dzuwa lapita,
  • Hymn 17 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 233 AMBUYE Mulungu,
  • Hymn 122 KUNALI munthu wa Mlungu,
  • Hymn 1615 Anakonda,
  • Hymn 1390 Nditamatu Ambuyangayu,
  • Hymn 169 M’manda nagonamo
  • Hymn 1714 Tiyeni, dzalireni nane,
  • Hymn 1700 Ambuye Mwini moyo,
  • Hymn 1568 Kudzoza kwanu kutipatsa
  • Hymn 723 Mundimvere, Mbuye wanga
  • Hymn 1592 Tsono mubwere inunso,
  • Hymn 1084 “Khala mwa Ine,” munachotsa tsoka,
  • Hymn 343 Auke,
  • Hymn 1342 Tadza kumtsinjeku
  • Hymn 465 ANA a Yerusalemu
  • Hymn 382 Mwadzoza mutu wanga ndi
  • Hymn 1299 Mzimu mndipatseko,
  • Hymn 1164 Tikakhulupira
  • Hymn 1461 Sing’anga ‘mkulu ndiye Yesu,
  • Hymn 253 Adzakhala pampandopo
  • Hymn 1048 Kumwamba ndiona Ambuyangayo,
  • Hymn 74 IDZA wolema,
  • Hymn 239 Akumwambawo
  • Hymn 1113 Mtima wa Mbuyako
  • Hymn 489 YESU ndiye Bwenzi lathu,
  • Hymn 1781 Timwimbire nyimbo,
  • Hymn 1744 Kale ophunzira ake
  • Hymn 1072 Mudzaze Yesu mtima wanga ndi chikondicho,
  • Hymn 843 M’maiko monse, zisi zomwe,
  • Hymn 1467 M’ulemerero mwake
  • Hymn 1709 Pamtandapo Ambuyeyo anafera ifetu,
  • Hymn 1807 Chithawa m’talitali
  • Hymn 860 Nthawi yina adzadzuka

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version