Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 375 YESU m’khale nafe

  1. Home   »  
  2. Hymn 375 YESU m’khale nafe

Hymn 375 YESU m’khale nafe

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 375 YESU m’khale nafe

 

YESU m’khale nafe
Nthaŵi yomweyi,
Kuti mphamvu zanu
Tilandirezi.

Mzimu Wakuyera
Mutipatsetu,
Mtima wathu wonse
Usakhale duu.

Moyo watsopano
Ulimbitse ’fe,
Mlungu wathu yemwe
Timdikirabe.

Post navigation

Previous: Hymn 374 NDI lokoma m’Mwambamo,
Next: Hymn 376 PAMTANDA Mbuye anafera,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 123 Koma mudzisungire chuma cha Kumwamba
  • Hymn 466 Yesu, muli pa chimpando
  • Hymn 270 Zoopsya zopambana
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 441 MBUYE, tikuthokozani,
  • Hymn 1813 Pochimwa anthu onsewo
  • Hymn 1122 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 239 TILI ndi mtendere
  • Hymn 1342 Tadza kumtsinjeku
  • Hymn 730 A! Yesu mwapangana
  • Hymn 577 Adagona m’ndyeromo
  • Hymn 1074 Mubweretu nomwe ‘Nu munatsika kalelo;
  • Hymn 640 Anakwatira kale
  • Hymn 46 O! ufulu tigwirizane
  • Hymn 1423 Oipa inu nonsetu,
  • Hymn 273 Mlungu akuyang’aniredi
  • Hymn 1536 Ndilira Mzimu leroli,
  • Hymn 526 Mnandidzera, Ambuye,
  • Hymn 1388 Tiimbire Mlungu wathu
  • Hymn 1276 Ndikhulupirira, Yesu, Inu nokhadi
  • Hymn 1719 Ku Mzinda wakuyerawo
  • Hymn 653 Nditsogolere m’njirayi
  • Hymn 1452 Inu akutopawo,
  • Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,
  • Hymn 119 Tamverani anthu inu,
  • Hymn 1748 Ambuye tsopano lino,
  • Hymn 65 Chisomo chodabwitsacho
  • Hymn 244 TIMVE za anamwali khumi,
  • Hymn 289 ANATILEMBA Yesu tikagwire nkhondo yake,
  • Hymn 636 Yehova Mlungu wathu,
  • Hymn 1638 Alinkudza wansoni Munthu
  • Hymn 460 E! ang’ono ndifetu,
  • Hymn 1162 Mumvetu abwenzi athu,
  • Hymn 998 Anatilemba Yesu tikagwire nkhondo yake,
  • Hymn 451 Yesu ndi Mbuyako,
  • Hymn 1825 Zobvuta zoopsa ndi zosaukazi
  • Hymn 4 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?
  • Hymn 594 Monga may’ asusuza
  • Hymn 1178 Mawu omwewo, nyimbo yomweyi,
  • Hymn 174 Haya, anzathu, itilinda nkhondo;
  • Hymn 620 Mphatso zonse zathu
  • Hymn 425 AKRISTU ndi abale, tiziyenderana tonse,
  • Hymn 1754 Ndiye akumbukira
  • Hymn 1808 Kutuma wabwereza,
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 763 Ndiponso m’manja chikhocho
  • Hymn 194 Kuli dziko labwino m’Mwamba
  • Hymn 905 Iwo asekera, iwo asekera,
  • Hymn 775 Mwa anthu onsewo
  • Hymn 976 Muyendenso kunka komwe,
  • Hymn 406 Kwa Yesu ndi kwabwinoko,
  • Hymn 169 M’manda nagonamo
  • Hymn 1467 M’ulemerero mwake
  • Hymn 1534 Mukonze mtima wangawu,
  • Hymn 1628 Dziko lino linaona
  • Hymn 861 Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi;
  • Hymn 907 Dziko labwinotu, dziko labwinotu,
  • Hymn 673 Mbwere Mzimu Wakuyera,
  • Hymn 879 Zokoma etu nthawizi”

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version