Hymn 1786 Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1786 Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga Amva pemphero ndi kulira kwanga, Namatchereza khutu nditapfuula, Andithandiza, nandipulumutsa.