Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

  1. Home   »  
  2. Hymn 390 A! YESU, ndapangana

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

 

A! YESU, ndapangana
Kutumikira ’Nu
Ndi moyo wanga wonse,
Mbuyanga ndinutu;
Mukhaletu pafupi
Masiku onsewo,
Sindidzaopa konse,
Mutsogolereko.

Ndikufuna kumva Inu,
E, Mawu anuwo,
Ndisamve za satana
Zonyenga zakezo;
Adani anga onse
Andizingiratu;
Mukhaletu pafupi,
Mundithangate ’Nu.

A! Yesu mwapangana
Ndi anthu anuwo
Adzakhala ndinu
Ku Dziko lanulo;
Inenso ndapangana
Ndisabwerere ’yi;
Mndipatse mphamvu yanu
Ambuye ndinudi.

Mundionetse, Yesu,
Mapazi anuwo,
Ndidzapondera awa
Munjira monsemo;
Ndithangateni ine
Ndisalefuke ’yi;
Mundilandire m’Mwamba
Ndikamwaliradi.

Post navigation

Previous: Hymn 389 NDIMAMVA njala, Yesu,
Next: Hymn 391 MUNDIMVERE, Mbuye wanga

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1297 Kumwamba komwe n’dzaimbira
  • Hymn 1113 Mtima wa Mbuyako
  • Hymn 49 Ndi ife akudziwa
  • Hymn 72 YESU wakukoma mtima,
  • Hymn 97 Maso ndi maso ndi Kristu,
  • Hymn 1058 Chimwemwe chija chamumtima
  • Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga
  • Hymn 1001 Mafumu atiuza tikaletse ukapolo,
  • Hymn 515 Kuphiri la ‘Zitona,
  • Hymn 238 MULUNGU wanga,
  • Hymn 1196 E! chikondi ndithu,
  • Hymn 1168 Aleluya, muyenera!
  • Hymn 1335 Wandifera Yesuyo
  • Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,
  • Hymn 736 Mndidyetse m’chipululu
  • Hymn 1549 Mtitsutse titachimwa
  • Hymn 299 “Posunga nkhosa ife
  • Hymn 1853 Etu ine, etu ine,
  • Hymn 868 Atate yemwe anatuma Mpulumutsi mmodzi
  • Hymn 739 Ndilibe wondithangata ‘ne ‘yi,
  • Hymn 64 LERO Kristu anauka,
  • Hymn 178 Machimo anga ngambiri
  • Hymn 576 Kondwerani nonsenu
  • Hymn 507 Yesu ndimkonda, akondanso ine,
  • Hymn 299 TIYENI, Akristu inu,
  • Hymn 854 Timlemekeze Mlunguyu
  • Hymn 727 Imfa ikandifikira,
  • Hymn 131 Lolani ana, mumve Mlungu,
  • Hymn 117 Atate wondipatsazo,
  • Hymn 670 Isaleke ntchito yake
  • Hymn 424 MTIDZUTSE, Mbuyetu,
  • Hymn 760 Usiku uja kalelo
  • Hymn 1828 Timtamande Iye ndi moyo wathunso
  • Hymn 581 Mtiphunzitse bwinotu,
  • Hymn 472 YESU, ndikabwera
  • Hymn 1483 Pakupempha ife pano,
  • Hymn 1484 Idzatu, idzatu
  • Hymn 1838 Ndiye Mbuye wa ambuye;
  • Hymn 1782 Poyamba paja analenga
  • Hymn 1633 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 625 Chaka chino mutipatse
  • Hymn 652 Munene Mbuye ‘nenetu,
  • Hymn 320 NDIKONDA Mlungu pomva Mbuye wanga
  • Hymn 236 Omvana ndi Yesu,
  • Hymn 179 TUMPHATUMPHA moyo wanga,
  • Hymn 1783 Tinasokera ngati nkhosa,
  • Hymn 1396 Ndi maso Ambuyathu
  • Hymn 1401 Imvani mawu ake, idzanitu,
  • Hymn 376 Adzadalitsa ‘fe
  • Hymn 118 Musaone zobvalazo,
  • Hymn 665 Pomangidwa anthu nayo
  • Hymn 6 Nanu akukuzani amithenga,
  • Hymn 1482 Tsopano inu ‘dzanitu,
  • Hymn 1852 Mbuye ndamva mwawazira
  • Hymn 197 Tidzatama Atate wathu
  • Hymn 1586 Mbuye Yesu timtamanda
  • Hymn 1781 Timwimbire nyimbo,
  • Hymn 986 Tiyeni anzathu
  • Hymn 410 MAWU akewo anamveka ponse,
  • Hymn 688 Anthu akum’mawa

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version