Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 294 POYESEDWA ine

  1. Home   »  
  2. Hymn 294 POYESEDWA ine

Hymn 294 POYESEDWA ine

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 294 POYESEDWA ine

 

POYESEDWA ine
Yesu mudzetu,
Mundipempherere
Ndisachimwetu.
Mukaona kuti
Ndilefukatu,
Mbuye mndilimbitse
Nazo mphamvutu.

Ndi zapansi pano
Ndikokedwadi,
Koma ndi chisoni
Mndiphunzitsedi;
Ndisaiŵalire
Za Getsemane,
Pena mtanda wanu
Yesu Mbuye ’Nu.

Mukandipweteka,
Ndipirirapo:
Nsembe yanga ndiyo,
Landirani ’yo.
Ndikachita mantha Sindithaŵa ’yi:
Mtima udzalimba,
Ndidzaima nji!

Pakumalizidwa
Moyo wangawu,
Pomwalira ine,
Mudze Mbuyetu.
Ndidzadzipereka
M’manja mwanumo:
Mpulumutsi Yesu
Mndilandireko.

Post navigation

Previous: Hymn 280 YESU, afuna iwe unke kwawoko,
Next: Hymn 301 MBUYE, ndapangana

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 198 CHITSIMECHO cha mwaziwo
  • Hymn 226 Nditama mwaziwo!
  • Hymn 9 Mpingo woyera wa kwa anthuonse
  • Hymn 1433 Lero lino ndi labwino;
  • Hymn 90 Ufuna kuleka kunyadako?
  • Hymn 277 GWIRA zintchito zako,
  • Hymn 828 Ndidzukanso m’mawa,
  • Hymn 666 Walitsani nyali yanu
  • Hymn 1747 Yesu aitana ife;
  • Hymn 105 Tiyamike Mbuye Yesu
  • Hymn 366 Anthu onse a padziko
  • Hymn 1135 Mulungu anditsogolera,
  • Hymn 370 KWACHA lero kwati mbee,
  • Hymn 559 Usikuwo woyerawo!
  • Hymn 131 MAWU a Mulungu awa,
  • Hymn 57 TIYENI, dzalireni nane,
  • Hymn 558 Mwanayo wa Mulunguyo
  • Hymn 1632 Ndi chiyembekezo ichi
  • Hymn 41 MKATI mwa zovuta zathu
  • Hymn 1310 Yesu wondikondadi,
  • Hymn 1394 Paphiri ndi padambo
  • Hymn 15 YEHOVA ndiye Mbusa wanga,
  • Hymn 560 Kale m’mzinda wachifumu
  • Hymn 865 Pakubweradi Woyesa tidzamlaka ifetu;
  • Hymn 1834 Chisomo ndi zokoma zake sizileka konse;
  • Hymn 28 Mbuye ndisaukadi,
  • Hymn 309 Mwa Mzimu mulowe mumitima yathu,
  • Hymn 390 A! YESU, ndapangana
  • Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
  • Hymn 167 Yendanitu, Wansembe wathu,
  • Hymn 881 Tili nazo zotiyesa,
  • Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu,
  • Hymn 1769 Ndiye amachitira
  • Hymn 116 Nkhosa zanga zimandimva
  • Hymn 393 Tilikuimba nyimbo yomweyi,
  • Hymn 1515 Ndikachimwa, Bukuli
  • Hymn 60 Chitetezo chachikulu
  • Hymn 742 Tikadya phando zaka zonsezi,
  • Hymn 209 Mdima ufika, dzuwa lalowa,
  • Hymn 157 Mbuye, Mzimu Woyera
  • Hymn 1764 Yesu ndinu Mbuye wathu,
  • Hymn 11 NDI mitima yokondwera,
  • Hymn 585 Alanditsa,
  • Hymn 1402 Mverani Iye ati: idzanitu;
  • Hymn 632 Tsopano tipereka mapemphero athu ano,
  • Hymn 94 Ndani anatiwombola?
  • Hymn 1499 Simbanitu mwachete
  • Hymn 488 M’MANJA a Yesu wanga
  • Hymn 1854 Tate msandipitirire,
  • Hymn 1233 Tsopano ndibukitsabe chikondi chanu chija
  • Hymn 403 NDIYIMBA ndi chimwemwe lero,
  • Hymn 975 Tiyeni, Akristu inu,
  • Hymn 567 M’nyumba zonse ponseponse
  • Hymn 1679 Tiyamike Dzina lake, Aleluya,
  • Hymn 247 MULUNGU anditsogolera,
  • Hymn 320 Ambuye, wakuti ndi mwaziwo
  • Hymn 308 AULENDO, munka kuti
  • Hymn 140 Panalitu wakudwala
  • Hymn 1235 Yesu wathadi
  • Hymn 861 Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi;

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version