Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 11 NDI mitima yokondwera,

  1. Home   »  
  2. Hymn 11 NDI mitima yokondwera,

Hymn 11 NDI mitima yokondwera,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 11 NDI mitima yokondwera,

 

NDI mitima yokondwera,
Mbuye wathu tiyamika.

E, chifundo chake chonse,
Ndi chosatha nthaŵi zonse.

Dzina lake tibukitsa,
Mlungu ndiye yekhayekha.

Mphamvu yake inalenga,
Dziko lonse ndi kumwamba.

Anatsogolera kale,
M’chipululu anthu ake.

Ndi chifundo atipenya,
Ife anthu osawuka.

Amaŵeta nyama zonse,
Zingasoŵe kanthu konse.

Tiimbire Mlungu wathu,
Waulemu ndi wamkulu.

Tithaŵire kwa Mulungu,
Ndiko tikapeze moyo.

Post navigation

Previous: Hymn 10 TSOPANO linoli,
Next: Hymn 12 NDITAMATU Ambuyangayu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 575 Taonani m’kholamo
  • Hymn 1658 Idza wolema,
  • Hymn 1374 Inu mumvere anyamatawo,
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,
  • Hymn 574 A! Yesu Mbuye wakuyera,
  • Hymn 991 Ndi zapansi pano
  • Hymn 341 PAKUPEMPHERATU
  • Hymn 98 YESU, Bwenzi la ochimwa,
  • Hymn 1063 Pokhala mtendere mu mtimangamu,
  • Hymn 630 Ena atsagana nafe
  • Hymn 713 Ambuye, Mwini zonsezi,
  • Hymn 1147 Khalani duu! Pakufa ifetu,
  • Hymn 936 Ukatha moyo wanga
  • Hymn 1564 Mufike monga moto wakuotcha zomwezo.
  • Hymn 1393 Nditamatu Ambuyangayu,
  • Hymn 314 TIYENI nonsenu okonda YESUYO,
  • Hymn 739 Ndilibe wondithangata ‘ne ‘yi,
  • Hymn 284 Yesu Mfumu Inu
  • Hymn 1639 Aleluya, aleluya,
  • Hymn 779 Yesu Mbuye wanga,
  • Hymn 725 Munafera ine kale
  • Hymn 1727 Pokumbukira mtandawo
  • Hymn 305 NDALIMVA dziko la m’talimo,
  • Hymn 1142 Tidzathawira kuti ‘fe
  • Hymn 785 Yehova adalitse ‘nu,
  • Hymn 431 Pompano pandikonda
  • Hymn 119 Tamverani anthu inu,
  • Hymn 846 Kristu wakuyeratu,
  • Hymn 605 Chifukwa cha zokoma mtima zonse za ulerezo,
  • Hymn 16 MTIMA wanga lemekeza,
  • Hymn 1108 Khala chete mtima wanga,
  • Hymn 564 Ndi chifukwa atikonda,
  • Hymn 453 Tiana ta Ambuye tili
  • Hymn 755 Pamene padzakhalapo
  • Hymn 75 MBUYE, mutsaganetu
  • Hymn 291 Ndi milomo yathu iyinso njanu,
  • Hymn 1130 Mbuyanga Yesu, mundigwire dzanja
  • Hymn 300 AKRISTU limbikani,
  • Hymn 942 Kaamba chisomo cha Mbuyathu
  • Hymn 250 MBUYANGA Yesu,
  • Hymn 232 Uchita kwombola,
  • Hymn 282 Ine ndili munthu
  • Hymn 1117 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 1717 Mtima wangawe, uyenera
  • Hymn 5 ATATE wa Kumwambako,
  • Hymn 566 Ana inu, ana inu,
  • Hymn 44 NTHAWIYO anam’gwira Yesu,
  • Hymn 27 LEMEKEZANI Yehova,
  • Hymn 378 KWEZANI mitu yanuyo,
  • Hymn 1141 Pakulekana ifetu
  • Hymn 1497 Simbani mobwereza,
  • Hymn 366 MADZULO aja kalero
  • Hymn 894 Mbuye, ndinu Mfumu yanga
  • Hymn 1036 Mtima wakufatsa
  • Hymn 1619 Adzabwera,
  • Hymn 1185 Imfa ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 466 OSANATU, osana,
  • Hymn 1468 Zobvala zake zonse
  • Hymn 177 Tate, ndili mwana wanu,
  • Hymn 615 Yamikani nonse ‘nu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version