Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 257 NJIRA yanga sindiziŵa,

  1. Home   »  
  2. Hymn 257 NJIRA yanga sindiziŵa,

Hymn 257 NJIRA yanga sindiziŵa,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 257 NJIRA yanga sindiziŵa,

 

NJIRA yanga sindiziŵa,
’Tate muikonza;
Komatu muzindikira
Kuti mundikonda.

M’mene mantha andigwira,
Andidetsa m’mtima,
Mbuye, ndithaŵire kwanu
Poti mundikonda.

Sindidziŵatu zamaŵa,
Koma sindiopa;
Ndidzakhulupira Inu
Kuti mundikonda.

Inde wakukonda ndinu;
Mawuwo oona
Andidzaza ndi chimwemwe:
Mlungu andikonda.

Post navigation

Previous: Hymn 256 NGATI mtima sumakonda
Next: Hymn 258 MWA ine, moyo wanga ndi Yesu

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1809 Yampatsa Nowa yemwe,
  • Hymn 440 ZIKOMO Ambuye wathu,
  • Hymn 790 Zimbalame zonsezi
  • Hymn 1738 “Senzani mtanda wanuwo.”
  • Hymn 1591 Sizitha ntchito zangazo,
  • Hymn 937 Chitsime chachikondi
  • Hymn 934 Mnamwalira Inu paja,
  • Hymn 484 Mutiletse, Mbuye,
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 273 USAFUNE chuma chokha,
  • Hymn 356 YESU Mbuye onani,
  • Hymn 23 Mvera mtima wanga ‘we
  • Hymn 1849 Nthawi zonse monga ‘Tate
  • Hymn 34 AMITHENGA a Mulungu,
  • Hymn 408 Oipa tili tonsefe;
  • Hymn 664 Komwe asauka anthu
  • Hymn 1018 Yesu afuna iwe unnke kwawoko,
  • Hymn 666 Walitsani nyali yanu
  • Hymn 76 E, MOYO wanga’we
  • Hymn 111 Nkhope yake ‘kabisika,
  • Hymn 1142 Tidzathawira kuti ‘fe
  • Hymn 698 Polenga dzikoli,
  • Hymn 1284 Kale ndinalira Inu,
  • Hymn 1387 Amaweta nyama zonse,
  • Hymn 411 Yesu adza kukundika
  • Hymn 256 NGATI mtima sumakonda
  • Hymn 38 ANGELO ayimba,
  • Hymn 170 YESU ponong’oneza, idzanitu;
  • Hymn 83 Mpulumutsi Wokondedwa,
  • Hymn 1698 Chinkana dziko lonselo
  • Hymn 291 ULENDO wachikhrisitu ngosawutsa ndithu,
  • Hymn 1795 A! chikondi chachikulu
  • Hymn 1344 Yamba ulendowo
  • Hymn 828 Ndidzukanso m’mawa,
  • Hymn 700 Mzimu woonadi
  • Hymn 725 Munafera ine kale
  • Hymn 465 Yesu atiuza tiwale pa
  • Hymn 339 Tipempha,
  • Hymn 377 ANTCHITO a Mulungu ’nu
  • Hymn 1298 Ndikhulupira ‘Nu,
  • Hymn 6 LEMEKEZA Mulungu ’Tate,
  • Hymn 244 Ndidze pafupi pa
  • Hymn 589 Koma ineyu
  • Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,
  • Hymn 862 Tidza kwa Mulungu Inu, ndinu wa chifundo;
  • Hymn 1619 Adzabwera,
  • Hymn 1525 Mbuye, mtiphunzitse
  • Hymn 349 MOSE anamenya thanthwe kawiri,
  • Hymn 1149 Chete! Chete!
  • Hymn 412 MOYO uli pafupi,
  • Hymn 1840 Ndiye M’busa wanga,
  • Hymn 133 Yesu watidzera, watidzera,
  • Hymn 139 Bwerani inu nonse, inu nonse,
  • Hymn 1779 M’dzikomo Ambuye
  • Hymn 819 Lero tigone,
  • Hymn 193 A! Kumwamba
  • Hymn 1599 Inde, ndifuna kumvatu
  • Hymn 50 PAUSIKU uja,
  • Hymn 151 Inde, Yesu, mulandira,
  • Hymn 378 Ku madzi ake odikha

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version