Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,

  1. Home   »  
  2. Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,

Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,

 

YANG’ANA mtanda wa Yesu,
Upeze moyo;
Chuma cha dziko chidzatha,
Yang’ana kwa Yesu.

Poyang’ana kwa Yesu Mbuye,
Pakuwona pamtanda wake,
Moyo ulipo.

Yesu alira pamtanda,
Kulilira ‘fe;
Kuti tilape zoipa,
Zomwe tichitazi.

Ambuye anatifera,
Pamtanda paja;
Kuti tikapeze moyo,
Kumwamba kwa Yesu.

Post navigation

Previous: Hymn 403 NDIYIMBA ndi chimwemwe lero,
Next: Hymn 405 POLENGA dzikoli

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1671 Akhululukira iwe,
  • Hymn 1354 Mzimu Woyera, m’mtimamo
  • Hymn 1172 Adzabweranso
  • Hymn 224 Atero ndaniyo?
  • Hymn 1416 Mbuye wanga ndilikumva,
  • Hymn 176 AITANA, aitana dziko lonse,
  • Hymn 719 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 68 M’MANDA, nagonamo
  • Hymn 372 DZUŴA la Mulungu
  • Hymn 15 Mbuye, chifundo chanu chitigwere
  • Hymn 366 Anthu onse a padziko
  • Hymn 979 Limbikani inu nonse,
  • Hymn 218 Mbuye Yesu ndi Atate,
  • Hymn 909 Ife tikondwera, ife tikondwera,
  • Hymn 1266 E, chimwemwe chachikulu, N’taperekadi
  • Hymn 24 “Ndakupeza womanga,
  • Hymn 245 Ngakhale kuthengo
  • Hymn 1379 Mulungu yemweyo
  • Hymn 988 Ndikhumba Mzimu wanu
  • Hymn 1524 Ndiwo alimbitsa
  • Hymn 766 Monga zomera zonsezo
  • Hymn 573 Ambuye, tikutamandani
  • Hymn 196 Tidzimba komweko nyimbo
  • Hymn 139 Bwerani inu nonse, inu nonse,
  • Hymn 425 Ine ndine mlendo
  • Hymn 752 Chakudya chakumwambachi
  • Hymn 1228 Lindikomera dzina la Ambuye Yesu wanga,
  • Hymn 171 M’manda munalibe
  • Hymn 90 Ufuna kuleka kunyadako?
  • Hymn 20 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 290 NAMONDWE wawuka,
  • Hymn 69 KONDWERANI dzuŵa lino,
  • Hymn 718 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 1413 Ndichitenji kukapeza
  • Hymn 1245 Ine ndidzakuonetsa
  • Hymn 687 Bukitsani mawunso
  • Hymn 1443 Ambuye Yesu anatsira
  • Hymn 842 Tipempha kuti Mpingo wanu
  • Hymn 359 TADZUKA mzimu wanga ‘we,
  • Hymn 1562 Mzimu Woyera, mudze mumitima mwathumo,
  • Hymn 439 Nthawi yaubwana yatha,
  • Hymn 1140 Paja athira Yesutu
  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 692 Paulendo wathu
  • Hymn 1581 Ndi nyimbo yabwino
  • Hymn 885 Mndimvetse chisoni
  • Hymn 137 UTHENGA wa Ambuye
  • Hymn 39 MUNASIYATU dziko lanulo,
  • Hymn 475 Mbuye ndikhaletu
  • Hymn 1365 Zozizwa za m’dziko,
  • Hymn 973 Tigwire nkhondo yomwe
  • Hymn 117 Atate wondipatsazo,
  • Hymn 74 IDZA wolema,
  • Hymn 1081 Ndikabisala mwanu
  • Hymn 307 ABALE anga ine ndikupita,
  • Hymn 344 ’TATE, ’Nu.
  • Hymn 1453 Mukana Iye bwanji,
  • Hymn 920 Yatha misoziyo,
  • Hymn 1130 Mbuyanga Yesu, mundigwire dzanja
  • Hymn 1857 Ndinagona mwa zoipa,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version