Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

  1. Home   »  
  2. Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

 

A! MUTU wakuyera,
Wolaswa wachisoni,
Abveka Inu anthu
Ndi minga ya udani;
Ambuye mwafokatu
Ndi masauko aja,
Mwatuŵa m’maso mwanu
Mumayerera kale.

Ambuye Mwini moyo,
Kokoma mnafumako;
Ndizizwa pomva mawu
Umo mwachitiramo.
Chisoni chija chanu
Ncha pamachimo anga,
Mwasaukira Inu
Kupalamula kwanga.

Nditani! Bwezi langa
Kulemekeza Inu
Chifukwa cha chifundo
Ndi imfa ija yanu?
Mundikhalitse wanu,
Wokhulupira inu;
Musandilole konse
Kufulatira Inu.

Pakufa ine Mbuye
Mukhaletu pafupi,
Mundithandize ine,
E, mudzandimasula;
Ndipenyetsetsa Yesu,
Ambuye Mfumu yanga,
Ndikafa ndine wanu,
Ndikhale nanu m’Mwamba.

Post navigation

Previous: Hymn 60 ZATHEDWA zonsetu
Next: Hymn 62 AMBUYE Yesu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 322 Walira Yesu m’dziko linoli,
  • Hymn 1300 Poyenda m’mdima bii,
  • Hymn 1243 Kodi mayi wobereka
  • Hymn 840 Ambuye munapatsa tsiku
  • Hymn 1008 Wakuchezacheza naye
  • Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu
  • Hymn 303 Ona pamtanda Yesuyo
  • Hymn 42 Masiku tikatsala ife
  • Hymn 702 Mbuye wathu mutipatsa
  • Hymn 1757 Udzadziwitsa anthu
  • Hymn 1372 Zam’madzi zonse zakuopsyazo,
  • Hymn 329 MUMZINDA wa Mulungu
  • Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu,
  • Hymn 817 Tibvomereze,
  • Hymn 867 Akristu ndi abale, tiziyenderana tonse,
  • Hymn 1587 Nditama Mlungu m’mtimamo,
  • Hymn 1549 Mtitsutse titachimwa
  • Hymn 556 Ndani pachimpandocho
  • Hymn 311 Tifuna kuchita chifuniro chanu,
  • Hymn 470 Mutiletse tisaname
  • Hymn 889 Pemphera m’mbanda kucha,
  • Hymn 136 Atumwi atummika, atumika,
  • Hymn 15 YEHOVA ndiye Mbusa wanga,
  • Hymn 69 Kwathu sipadziko, ndingopitirira,
  • Hymn 1769 Ndiye amachitira
  • Hymn 283 AMBUYE m’chipululu,
  • Hymn 1051 Zin’sowa indedi
  • Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,
  • Hymn 754 Ndi mtanda uli m’maso mbuu,
  • Hymn 1333 Idzatu kwa Yesuyo,
  • Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo
  • Hymn 151 UKAPENYA kwa Yesu uliko moyoko,
  • Hymn 1026 Inde nditaya chumacho,
  • Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu
  • Hymn 1739 Ife timakufunani
  • Hymn 103 Bwenzi lathu ndinutu,
  • Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,
  • Hymn 668 Achisoni, obvutidwa,
  • Hymn 22 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 630 Ena atsagana nafe
  • Hymn 1431 Lero lino m’bale wanga,
  • Hymn 440 ZIKOMO Ambuye wathu,
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 774 Tibatizidweko,
  • Hymn 1481 Timsankhe Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 660 Tumizani kuunikako,
  • Hymn 125 Aliponso mabvuto, ena ndi oipa;
  • Hymn 174 Haya, anzathu, itilinda nkhondo;
  • Hymn 207 Malo alimo m’nyumba ya Yesu,
  • Hymn 192 Apita anzathu dzuwa lino Kosaoneka,
  • Hymn 1199 Ndikhumba ine ndithu
  • Hymn 323 Tiwaliretu, tiwaliretu
  • Hymn 360 KRISTU wakuyeratu,
  • Hymn 108 Tikondwera ife tonse
  • Hymn 1784 Komweko titasaukira,
  • Hymn 1293 Chitsimecho cha mwaziwo
  • Hymn 184 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 122 Musadziunjikire chuma cha padziko,
  • Hymn 179 Ndinachimwa poganiza
  • Hymn 424 Yesu, mndiyeretse,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version