Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

  1. Home   »  
  2. Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 61 A! MUTU wakuyera,

 

A! MUTU wakuyera,
Wolaswa wachisoni,
Abveka Inu anthu
Ndi minga ya udani;
Ambuye mwafokatu
Ndi masauko aja,
Mwatuŵa m’maso mwanu
Mumayerera kale.

Ambuye Mwini moyo,
Kokoma mnafumako;
Ndizizwa pomva mawu
Umo mwachitiramo.
Chisoni chija chanu
Ncha pamachimo anga,
Mwasaukira Inu
Kupalamula kwanga.

Nditani! Bwezi langa
Kulemekeza Inu
Chifukwa cha chifundo
Ndi imfa ija yanu?
Mundikhalitse wanu,
Wokhulupira inu;
Musandilole konse
Kufulatira Inu.

Pakufa ine Mbuye
Mukhaletu pafupi,
Mundithandize ine,
E, mudzandimasula;
Ndipenyetsetsa Yesu,
Ambuye Mfumu yanga,
Ndikafa ndine wanu,
Ndikhale nanu m’Mwamba.

Post navigation

Previous: Hymn 60 ZATHEDWA zonsetu
Next: Hymn 62 AMBUYE Yesu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 19 MULUNGU akhale nawo,
  • Hymn 381 Chakudya changa chabwino
  • Hymn 474 MPULUMUTSI, Mbusa wathu,
  • Hymn 1073 Mwa ine myatse moto wanu wakuyera mbuu,
  • Hymn 480 TIANA ife tingofoka,
  • Hymn 729 Ndifuna kumva Inu,
  • Hymn 157 INU nonse ovutidwa,
  • Hymn 453 A! MULUNGU
  • Hymn 877 Zokoma ndithu nthawizi
  • Hymn 1741 Yesu munalaswa m’mtima,
  • Hymn 609 Zanu zapansi nzokoma Mbuye; tikondwera ‘fe,
  • Hymn 151 Inde, Yesu, mulandira,
  • Hymn 1677 Zomkweza zili m’Mwamba,Aleluya
  • Hymn 1011 M’mawa tizifesa
  • Hymn 545 Anatifera tonsefe
  • Hymn 90 WINA atikonda ife,
  • Hymn 1135 Mulungu anditsogolera,
  • Hymn 492 DZIKO lilipolo
  • Hymn 1559 Wotsogolera, munditsogolere
  • Hymn 790 Zimbalame zonsezi
  • Hymn 1078 Khalatu woyera
  • Hymn 681 Ankhondo a Mulungu ‘nu, yendani m’njiramo,
  • Hymn 15 YEHOVA ndiye Mbusa wanga,
  • Hymn 825 Mpatse ana ‘ng’ono
  • Hymn 154 SING’ANGA ‘mkulu ndiye Yesu,
  • Hymn 1438 Yesu akukonda,
  • Hymn 176 Mleke mdaniyo, mwimbe m’njiramo
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 309 Mwa Mzimu mulowe mumitima yathu,
  • Hymn 1203 Zambiri zangazo
  • Hymn 1129 Mbuyanga Yesu, ndikapanda Inu
  • Hymn 1022 Mbuye, nditsate bwanjiko?
  • Hymn 1313 Zindichulukirazi
  • Hymn 1630 Anthu anu amafoka,
  • Hymn 1551 Mukhale m’kati mwathu,
  • Hymn 1595 Ndani mwa abale athu
  • Hymn 1730 Anapeputsidwako,
  • Hymn 242 NDIIMBA mumtima mokondwa,
  • Hymn 295 Kubadwa kwa Yesu
  • Hymn 1147 Khalani duu! Pakufa ifetu,
  • Hymn 785 Yehova adalitse ‘nu,
  • Hymn 1729 Munthu Wazisoniyo
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 6 LEMEKEZA Mulungu ’Tate,
  • Hymn 714 Dzuwa ndi mvula yonseyo
  • Hymn 316 NDAMVATU kuti tifika komweko
  • Hymn 1123 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 505 Ndikondwa kuti Atate wam’Mwamba
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 1243 Kodi mayi wobereka
  • Hymn 291 Ndi milomo yathu iyinso njanu,
  • Hymn 16 Chikhulupiriro chathu
  • Hymn 19 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 120 MUNDINYEMERE ’ne
  • Hymn 1175 Sindinanyengedwa konse,
  • Hymn 1728 Zofuna zanga zonsezo
  • Hymn 1069 Zochimwa zathu m’mtimamo
  • Hymn 499 TIKUTHA kupemphera,
  • Hymn 335 KWATHU sipadziko, ndingopitilira,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version