Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

  1. Home   »  
  2. Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

 

KALE m’mzinda wachifumu
Munalimo m’kholamo,
Momwe mkazi anaika
Mwana wake m’ndyeromo.
Ndiye mkaziyo Mariya,
Yesu Kristu Mwanayo.

Uyu ’natsikira kuno,
Mlungu Mbuye wathuyo;
Anabadwa uyu m’khola
Anagona m’ndyeromo.
Mwa osoŵa ndi oipa
Yesu anakhalamo.

Mwa ubwana wake wonse
Anakula m’mtima phee!
Anakonda, anafatsa,
Amay’ wake namvabe;
Ndipo ana nonsenu,
Mukamtsate bwinotu.

Ndipo Mwana uyu Yesu
Anakulakulabe;
Ndi wamng’ono ndi wofoka,
Anagona enawo.
Nsoni zathu anazimva
Ndi chimwemwe chathunso.

Ndi chifukwa atikonda,
Tidzampenya masowa,
Kuti Mwanayo wofatsa
Ndiye Mwini m’Mwambamo;
Atengera ana ake
Komwe adapitako.

Koma sitimpenya m’khola
Muli ng’ombe momwemo;
Ayi, tidzamwona m’Mwamba
Muli Mlungu ’Tatewo.
Ana akuyera mbuu
Adzamzunguliratu.

Post navigation

Previous: Hymn 456 ANA inu, ana inu,
Next: Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 43 Ulendo wathu ukadzatha
  • Hymn 1070 Mthandize Mbuye, timvetu,
  • Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!
  • Hymn 1322 Ntchito zanga zonsezo
  • Hymn 985 Zonse zapadziko
  • Hymn 1461 Sing’anga ‘mkulu ndiye Yesu,
  • Hymn 1281 Ndikhulupirira, Yesu, mndibvomereko;
  • Hymn 140 NDINAMIRA m’machimo, wosaonekanso,
  • Hymn 1030 Tioperanji ifetu?
  • Hymn 76 E, MOYO wanga’we
  • Hymn 685 Tamva mawu amwewo
  • Hymn 1065 Ngakhale Satana andizunza ‘ne,
  • Hymn 577 Adagona m’ndyeromo
  • Hymn 551 Ndani kodi Munthuyo
  • Hymn 1043 Mbiri yake ubukitse,
  • Hymn 211 TIDZALAKALAKA kuwonana naye,
  • Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,
  • Hymn 776 Tikondwereratu
  • Hymn 563 Ndipo Mwana uyu Yesu
  • Hymn 936 Ukatha moyo wanga
  • Hymn 1792 Mulungu ndiye wachifundo,
  • Hymn 1471 Ukapenya kwa Yesu uliko moyoko,
  • Hymn 371 Mulungu, anthu ‘fe
  • Hymn 732 1 Ndinamva njala, Yesu,
  • Hymn 628 E! chisomo chosaleka
  • Hymn 192 Apita anzathu dzuwa lino Kosaoneka,
  • Hymn 1381 Ndi mitima yokondwera
  • Hymn 1805 Anafa m’mvula muja
  • Hymn 743 Mudze, anthuni, talawani ‘nu
  • Hymn 1347 Akukonda, akukonda,
  • Hymn 368 MULUNGU wanga, Dzuŵatu
  • Hymn 236 NDIDZIWITSITSA
  • Hymn 327 NTCHITO yonse yakeyo
  • Hymn 385 SINDILI woyenera ’ne,
  • Hymn 507 Yesu ndimkonda, akondanso ine,
  • Hymn 795 Sitinanyalanyalaza
  • Hymn 289 Ndi manja athu awa nawo nganu,
  • Hymn 674 Anthu onse taukani,
  • Hymn 4 INU Mulungu, tikuyamikani;
  • Hymn 1750 Ndi nyali yakuwalitsa
  • Hymn 291 ULENDO wachikhrisitu ngosawutsa ndithu,
  • Hymn 854 Timlemekeze Mlunguyu
  • Hymn 150 Ndisauka, sindiona;
  • Hymn 1178 Mawu omwewo, nyimbo yomweyi,
  • Hymn 256 NGATI mtima sumakonda
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 334 KULI dziko labwino M’mwamba,
  • Hymn 262 Tumphatumpha moyo wanga,
  • Hymn 73 M’SANDIPITILIRE Yesu,
  • Hymn 841 Mukhale, mukhale,
  • Hymn 1329 M’tali mutali m’phirimo
  • Hymn 956 Mbuye munditsogolere,
  • Hymn 983 Nkhondo ya Satana
  • Hymn 988 Ndikhumba Mzimu wanu
  • Hymn 20 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 651 Ikhale ngati nyali
  • Hymn 326 Yesu, Bwenzi la ochimwa,
  • Hymn 453 A! MULUNGU
  • Hymn 974 Tsopano timenyana
  • Hymn 168 NDINGANENE malilime,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version