Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

  1. Home   »  
  2. Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

 

KUNALI munthu ku Yeriko,
Dzina lake Zakeyu;
Anali munthu wamkulu,
Wokhometsa misonkho.

(M) Kunali Zakeyu,
(O) Ku Yeriko,
(M) Nafunafuna,
(O) Kuwona Yesu,
(M) Koma chifukwa,
(O) Cha khamulo,
Anakwera mumtengo.

Paulendowo Ambuyeyo,
Anafika pamtengo;
Nayang’ana m’mwamba muja,
Anawona Zakeyu,

Ambuye Yesu nanenadi,
“Fulumira nutsike;
Lero lino ndiyenera,
Kukhala m’nyumba mwako.”

Zakoyuyo mofulumira,
Anatsika mumtengo,
Anam’tenga Mbuye Yesu,
Kuti akam’chereze,

Anadandauladi ena,
“Ambuye wachitanji?
Bwanji Iye analowa,
M’nyumba ya wochimwayo?”

Zakeyuyo pakumva ichi,
Anawuza Ambuye:
“Theka la chuma changacho,
Ndidzapatsa osowa.”

Leronso chipulumutsochi,
Chagwera m’nyumba yathu;
Tilape zoipa zathu,
Kutí tipulumuke.

Post navigation

Previous: Hymn 213 INE ndili ndi manyazi
Next: Hymn 215 TATE ndili mwana wanu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1821 Angelo amazinga nyumba
  • Hymn 161 Tibwera ndi tianato
  • Hymn 1055 E, mtima watsopano ndi
  • Hymn 460 KULI kaphiri m’talimo
  • Hymn 1576 Khamulo liliko
  • Hymn 1314 Mulungu ali nane!
  • Hymn 288 HAYA! ’nzanga taonani
  • Hymn 1035 Mphamvu zathu zonse
  • Hymn 140 Panalitu wakudwala
  • Hymn 593 Yesu, munditsogoza
  • Hymn 19 MULUNGU akhale nawo,
  • Hymn 1442 Khulupira mawu onse
  • Hymn 845 Ufumu wanu, Mbuye Yesu,
  • Hymn 216 NDISAUKA, ndinachimwa,
  • Hymn 229 Woba wakufa ‘napenya
  • Hymn 597 Mlungu ali nane
  • Hymn 1186 Yesu anafa pamtandapo,
  • Hymn 1713 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 1310 Yesu wondikondadi,
  • Hymn 40 Padziko pano tikhalira
  • Hymn 187 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 137 Yesu Mpulumutsi, Mpulumutsi
  • Hymn 1410 Nthawi zonse mufunabe
  • Hymn 852 Munkhani zako zonsetu
  • Hymn 1321 Thanthwe long’ambikatu,
  • Hymn 418 M’manja Yesu wanga
  • Hymn 697 Zolengedwa zonse zidze
  • Hymn 223 ATI Yesu Mbuyeyo:
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu
  • Hymn 533 Ananu, ziimbani,
  • Hymn 477 YESU, muli pa chimpando
  • Hymn 911 Mokhala mokhamokha
  • Hymn 1385 Anatsogolera kale
  • Hymn 994 Limba mtima mbale wanga,
  • Hymn 634 Mtifungatire ndi mapiko paulendo pathu,
  • Hymn 1448 Yesu ndiye Bwenzi lanu,
  • Hymn 1128 Mbuyanga Yesu, mundisunge ine
  • Hymn 462 ANANU, ziimbani,
  • Hymn 1464 Nditama Nsembe ya Mulungu,
  • Hymn 347 Mfumu iyi,
  • Hymn 365 Monga m’Mwamba mupambana
  • Hymn 310 MBUYE munditsogolere,
  • Hymn 983 Nkhondo ya Satana
  • Hymn 27 LEMEKEZANI Yehova,
  • Hymn 933 M’mene imfa yathu idza,
  • Hymn 1282 Ndilinkudza kwa Ambuye,
  • Hymn 783 Antchito a Mulungu ‘nu
  • Hymn 419 ANYAMATA a Mulungu,
  • Hymn 1194 Padziko lapansi
  • Hymn 1211 Mwakhulupiriradi
  • Hymn 1179 N’kamvera Yesu ndikakondwera,
  • Hymn 284 Yesu Mfumu Inu
  • Hymn 26 “Ndakukonda ku imfa
  • Hymn 278 TITHAŴIRENJI ifetu
  • Hymn 274 YESU and’itana,
  • Hymn 472 YESU, ndikabwera
  • Hymn 253 YESU ndinutu wanga m’njira zonse,
  • Hymn 541 Ana inu, yamikani
  • Hymn 1058 Chimwemwe chija chamumtima
  • Hymn 235 ADALITSIKA munthuyo,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version