Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 302 NDIDZE pafupi pa

  1. Home   »  
  2. Hymn 302 NDIDZE pafupi pa

Hymn 302 NDIDZE pafupi pa

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 302 NDIDZE pafupi pa

 

NDIDZE pafupi pa
Mlungu wanga,
Ngakhale pamtanda
Mundikweza;
Koma ndiimbabe
Mbuye mndikhalitse,
Mbuye mndikhalitse,
M’fupi Ndinu.

Ngakhale kuthengo
Ndasokera,
M’mdima ndigonapa
E, pamwala;
Koma m’kulotako
Ndiyandikizanso,
Ndiyandikizanso
M’fupi Ndinu.

Pajapo ndipenya
Pokwerapo,
Angelo atsika
Kumwambako,
Ndiwo akodola
Kuti ndikabwere,
Kuti ndikabwere
M’fupi Ndinu.

Tsopano poukanso
Wokondwatu,
Ndipeza pomwepo
Pali Mlungu;
Ndipo masautso
Andisendezanso,
Andisendezanso,
M’fupi Ndinu.

Pena pakufadi,
N’kwera m’Mwamba,
Dzuŵa ndi nyenyezi
Zitsalira;
Pomwe ndiimbanso,
Ndidza pafupi pa,
Ndidza pafupi pa
Mlungu wanga.

Post navigation

Previous: Hymn 301 MBUYE, ndapangana
Next: Hymn 303 MEMA nkhondoyo, wadza mdaniyo,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 525 Afike masiku
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,
  • Hymn 148 Ndisauka, ndimasowa
  • Hymn 1621 Yang’anani anthu onse,
  • Hymn 1560 Mthandizi ndinu, mndithangate ine
  • Hymn 889 Pemphera m’mbanda kucha,
  • Hymn 1834 Chisomo ndi zokoma zake sizileka konse;
  • Hymn 98 Ndidzamwona maso ndi maso
  • Hymn 1687 Alonda onsewo
  • Hymn 1252 Pakukumbukira zanga
  • Hymn 608 Maluwa abwino aphuka m’mapiri ndi m’madambomo,
  • Hymn 1509 Mkate wamoyowo
  • Hymn 1117 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 757 Sindili woyenera ‘ne;
  • Hymn 1516 Pakudera nkhawa ‘ne,
  • Hymn 1242 Ku zoipa zonse zako,
  • Hymn 192 Apita anzathu dzuwa lino Kosaoneka,
  • Hymn 479 Munanena mulandira
  • Hymn 1625 Ife tonse tikumbuke
  • Hymn 192 ZAKEYU mkulu wa misonkho,
  • Hymn 255 Pakuona imfayo
  • Hymn 1601 Zina za Yesu ndimvetu,
  • Hymn 1240 Ndilikuva m’mtima mwanga
  • Hymn 465 Yesu atiuza tiwale pa
  • Hymn 54 MUNTHU wazisoniyo,
  • Hymn 1817 Ndi m’munda muja chete, phee!
  • Hymn 491 N’takafika kwanu
  • Hymn 1274 Chisoni andichotsera Mbuyeyu,
  • Hymn 1120 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 35 KODI mwaona chiyani,
  • Hymn 329 Yesu atonthoza mtima
  • Hymn 424 MTIDZUTSE, Mbuyetu,
  • Hymn 477 YESU, muli pa chimpando
  • Hymn 1561 Mzimu Woyera, n’dzipereka ndense,
  • Hymn 896 Mbuye, ndinalema ine,
  • Hymn 106 Ife, tapulumukadi,
  • Hymn 1407 Tula mtolo wako
  • Hymn 685 Tamva mawu amwewo
  • Hymn 112 ELISA mneneri,
  • Hymn 1762 Anamva abusa omwe
  • Hymn 1275 Mtima ‘we siya ndi Yesu nsonizi,
  • Hymn 108 MBUYE wondipulumutsa,
  • Hymn 1288 Yesu mundimve, ndikuliratu,
  • Hymn 324 TIKAGWIDWA ndi chisoni,
  • Hymn 311 VALANI zida tizinka kwathuko,
  • Hymn 1720 Padzanja lachifundolo
  • Hymn 1777 Mulungu wamkulu
  • Hymn 807 Mpulumutsi tikagona
  • Hymn 155 UTHENGA wa Mulungu
  • Hymn 1013 Tizifesa m’dzuwa,
  • Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,
  • Hymn 495 Wonga Inu ndikhaledi,
  • Hymn 1565 Mufike monga ngati njiwa yamtenderewo,
  • Hymn 368 MULUNGU wanga, Dzuŵatu
  • Hymn 620 Mphatso zonse zathu
  • Hymn 1629 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 1673 Lambira Yesuyo
  • Hymn 306 Ona Mwanawanakhosayo
  • Hymn 448 Yesu ndi wofatsa,
  • Hymn 659 Anthu ali m’mdima akuitanitsa

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version