Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 450 YESU, munditsogoza

  1. Home   »  
  2. Hymn 450 YESU, munditsogoza

Hymn 450 YESU, munditsogoza

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 450 YESU, munditsogoza

 

YESU, munditsogoza
M’njira yanga yonseyo;
Wakunditsogozatu
Ndinu, mundisungetu;
Inde, paulendowo
Mundisunge kolimba.

Monga may’asusunza
Mwana wake polira,
Wakunditonthozatu
Ndinu, munditonthoze,
Ine, m’njira yanuyi
Munditsogoleretu.

Mbuye, ndinu wamphamvu,
Mumatola ananu.
Anthu onse pansipa
Ali otaikatu;
Muchitire chifundo,
Muŵatole onsewo.

Post navigation

Previous: Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,
Next: Hymn 451 MLUNGU alinane;

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 96 MTIMA wanga uyamiketu,
  • Hymn 1110 Mulungu wanga,
  • Hymn 799 Inu Mlungu kalelo
  • Hymn 42 “SENZANI mtanda wanuwu,
  • Hymn 240 YESU ndiye Mbuye wanga,
  • Hymn 248 Pena pakufadi,
  • Hymn 422 Kwathu nkopambana,
  • Hymn 119 Tamverani anthu inu,
  • Hymn 715 Mwapatsa Mwana wanu, ndi
  • Hymn 152 AMBUYE wathu Yesu
  • Hymn 365 DZUŴA lapita,
  • Hymn 12 Kumva milandu yathu mudzabwera
  • Hymn 30 Tamandani Mbuye,
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 856 Kuunika kuoneka
  • Hymn 1505 Ndikampeza, ndikamtsata
  • Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee!
  • Hymn 773 Mtsinje woyerawo
  • Hymn 760 Usiku uja kalelo
  • Hymn 1123 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 359 Tonse timyamiketu,
  • Hymn 1529 Mndithandize kukondana
  • Hymn 189 Koma Iye wandipeza;
  • Hymn 1293 Chitsimecho cha mwaziwo
  • Hymn 1702 Pakufa ine Mbuye
  • Hymn 460 E! ang’ono ndifetu,
  • Hymn 84 Aleluya, Aleluya,
  • Hymn 447 Usachimwe konse,
  • Hymn 681 Ankhondo a Mulungu ‘nu, yendani m’njiramo,
  • Hymn 842 Tipempha kuti Mpingo wanu
  • Hymn 413 Yesu ndiye Bwenzi lathu,
  • Hymn 212 NDI MISOZI, ndi chisoni,
  • Hymn 1248 ‘Dzanitu Wamphamvu yonse,
  • Hymn 566 Ana inu, ana inu,
  • Hymn 1745 Yesu aitana ife:
  • Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
  • Hymn 394 TATENGA mphatso zotani?
  • Hymn 450 Koma usalole
  • Hymn 198 M’dziko lino tikhalamo
  • Hymn 245 Ngakhale kuthengo
  • Hymn 924 Kodi uli ndi chisoni
  • Hymn 51 Mbuye dalitsani Afrika,
  • Hymn 468 NDIKONDWA kuti
  • Hymn 707 Dalitseni, Mbuye, zonse
  • Hymn 235 Kumwamba ndikaimbanso
  • Hymn 145 MBIRI yakale lomwe
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 26 “Ndakukonda ku imfa
  • Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!
  • Hymn 1562 Mzimu Woyera, mudze mumitima mwathumo,
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 539 Anafika ‘kazi omwe
  • Hymn 52 POTULUKA m’mudzimo
  • Hymn 515 Kuphiri la ‘Zitona,
  • Hymn 269 Atate ‘nu, amayi ‘nu, nonsenu,
  • Hymn 273 USAFUNE chuma chokha,
  • Hymn 147 Ndisauka, ndinachimwa,
  • Hymn 1618 Anakwera,
  • Hymn 1823 Opani Iye, nimuleke
  • Hymn 1187 M’mitima mwathu mwakhala mbee!

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version