Chichewa Christian Hymns
Hymn 421 ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,
ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,
Unikani! Unikani!
Alikumwazika
Mungawalanditse,
Unikani! Unikaní!
Tumizani kuunikako,
Kuwoneketu kwa onsewo;
Tumizani kuunikako,
Nthawi zonsedi kuwaletu.
Tamva aku
Makedon’yako atero,
Unikani! Unikani!
Tititu, Ambuye tizinka komweko,
Unikani! Unikani!
Tisaleme pakuchita zabwinozi,
Unikani! Unikani!
Tidziunjikire ngale za Kumwamba,
Unikani! Unikani!