Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

  1. Home   »  
  2. Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

 

MBUYE wathu, mutipatsa
Zonse tili nazozo,
Mutikomeratu mtima
Osaleka konseko,
Mutikonda, mutisunga,
Mutisamalira ’fe.

Dzuŵa, madzi, kudya, mpweya,
Moyo, zonse nzanuzi,
Si za ife, nzaulere,
Tingozilandiradi;
Zifumira kwa Aate
Wotikondakondatu.

Monga tilandira, Mbuye,
Mtiphunzitse tonsefe
Tipere chuma chathu
Ndi kusangalalatu;
Zakukhala m’manja mwathu
Tiziyese nzanudi.

Tikhaletu nawo, Mbuye,
Mtima wosauma ’yi
Ndi wofatsa ndi wabwino
Ndi woyerayeradi,
Kuti tiyenere Dzina
La Mbuyathu Yesuyo.

Tisaiwalire ’bale
Athu osadziŵa ’Nu,
Akulira ndi odwala
Tiŵapemphereratu;
Titsanzenso Mbuye Yesu
Ndi k’ŵathangatira ’wo.

Dalitseni, Mbuye, zonse
Zomwe taperekazi,
Mzilandire, nsembe yathu,
Mziyeretse Inudi
Ndi mitima yathu yonse
Tikuyamikirani.

Post navigation

Previous: Hymn 396 PETURO ’nafunsa Hananiya:
Next: Hymn 398 KODI mbale wasimba zachikhululukiro,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1557 M’phunzitsi, ndinu mudziwitse ine
  • Hymn 286 Atate, tifika pamaso panu;
  • Hymn 1525 Mbuye, mtiphunzitse
  • Hymn 77 Ndipereka zanga zonse,
  • Hymn 279 Mbwere mudzamve nonse
  • Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,
  • Hymn 1685 Nla Mlungu dzuwali;
  • Hymn 1252 Pakukumbukira zanga
  • Hymn 1579 Akhala mafumu
  • Hymn 567 M’nyumba zonse ponseponse
  • Hymn 251 NDIFUNA Yesuyo,
  • Hymn 1663 Yesu Mbuye,
  • Hymn 1639 Aleluya, aleluya,
  • Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,
  • Hymn 1228 Lindikomera dzina la Ambuye Yesu wanga,
  • Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee!
  • Hymn 850 Pemphero, pemphero,
  • Hymn 1419 Amayi ‘nu, amayi ‘nu,
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 357 TAMANDANI Mbuye,
  • Hymn 266 Ukondwere moyo wanga,
  • Hymn 1634 Pakwitana Mbuye wanga
  • Hymn 124 Aliponso adani am’kati ndi akunja;
  • Hymn 1715 Kodi misozi itisowa,
  • Hymn 437 Yesu ndiye Mbusa,
  • Hymn 1521 Poyensedwa ife
  • Hymn 1136 Mulungu anditsogolera
  • Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
  • Hymn 809 Madzulo aja kalelo
  • Hymn 737 Mommuno, Mbuye, tionanetu,
  • Hymn 574 A! Yesu Mbuye wakuyera,
  • Hymn 1773 Monga anapangana
  • Hymn 174 YESU wathu Mbuyeyo
  • Hymn 70 Mbuye ndinu bwenzi langa ndithu,
  • Hymn 1376 Akulu nonse ndi mafumu ‘nu,
  • Hymn 120 Lekani kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 1089 Ndionetsere kuunika
  • Hymn 1075 Ndikhazikike inetu, mumtima muli mwai,
  • Hymn 1160 Ndinakhala wakuipa,
  • Hymn 385 SINDILI woyenera ’ne,
  • Hymn 1486 M’dziko lino pansi pano
  • Hymn 1453 Mukana Iye bwanji,
  • Hymn 696 Ufumu wake udalitsa
  • Hymn 83 MBUYEYO adzabwera,
  • Hymn 546 Kulibe wokwanira ‘yi
  • Hymn 337 ‘Tate ‘Nu,
  • Hymn 502 Ndikonda mbiri yomwe
  • Hymn 700 Mzimu woonadi
  • Hymn 541 Ana inu, yamikani
  • Hymn 746 Imfa ndi mdima zinathawa zii!
  • Hymn 1000 Amatininkha zida zoteteza mtima, ndizo:
  • Hymn 1048 Kumwamba ndiona Ambuyangayo,
  • Hymn 293 LIMBA mtima mbale wanga
  • Hymn 1445 Tiyeni tonse, tinkeko
  • Hymn 204 NDASIYA zonse ndi Yesu kalelo,
  • Hymn 231 Mwazi wa Yesu wokondwa
  • Hymn 390 Lalowa dzuwa, kwada bii!
  • Hymn 861 Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi;
  • Hymn 762 “Ndi thupi lopatsidwali
  • Hymn 691 Akukhala kunja,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version