Chichewa Christian Hymns
Hymn 139 MLUNGU anapatsa moyo,
MLUNGU anapatsa moyo,
Moyo, moyo wosatha;
Mlungu anapatsa moyo,
Anapatsa moyo wosatha.
Anthu anakana moyo,
Moyo, moyo wosatha;
Anthu anakana moyo,
Anakana moyo wosatha.
Yesu apatsanso moyo,
Moyo, moyo wosatha;
Yesu apatsanso moyo,
Apatsanso moyo wosatha.
Kodi mwalandira moyo,
Moyo, moyo wosatha?
Kodi mwalandira moyo,
Mwalandira moyo wosatha?
Inde, ndalandira moyo,
Moyo, moyo wosatha;
Inde, ndalandira moyo,
Ndalandira moyo wosatha.