Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 143 KONZA mtima iwe mbale,

  1. Home   »  
  2. Hymn 143 KONZA mtima iwe mbale,

Hymn 143 KONZA mtima iwe mbale,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 143 KONZA mtima iwe mbale,

 

KONZA mtima iwe mbale,
Pakuleka tchimo;
Siya zonse uzikonda,
Ndikutsata Yesu.

Konza mtima wako lero,
Yesu alowemo;
Ndipo usachedwe iwe,
Taata Yesu lero.

Imva kuyankhula kwake,
Mawu a chikondi;
Ayankhula iwe lero,
Kuti upumule.

Nthawi ya chisomo m’dziko,
Ndi inotu mbale;
Yom’dziwatu Mpulumutsi,
Ukali ndi moyo.

Post navigation

Previous: Hymn 142 MULUNGU aŵakonda anthu
Next: Hymn 144 AMENE adzavomereza ndithu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 817 Tibvomereze,
  • Hymn 274 E! tidzakomanansotu
  • Hymn 557 Usikuwo woyerawo!
  • Hymn 311 VALANI zida tizinka kwathuko,
  • Hymn 458 Anyamata inutu,
  • Hymn 402 M’mtima mwangamu mlowemo,
  • Hymn 636 Yehova Mlungu wathu,
  • Hymn 133 NSEMBE yake ya Kaini,
  • Hymn 560 Kale m’mzinda wachifumu
  • Hymn 18 POKHALA Inu
  • Hymn 156 OKOMA ndiwo mawu
  • Hymn 1726 Linadetsedwa dzuwa bii!
  • Hymn 1567 Mubwere Mzimu Wakuyera,
  • Hymn 855 Aulendo amayenda
  • Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,
  • Hymn 1807 Chithawa m’talitali
  • Hymn 1412 Imfa idzafika msanga;
  • Hymn 1097 Njira yanga sindidziwa,
  • Hymn 103 MPUME pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 1662 Msandipitire, Yesu,
  • Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
  • Hymn 1371 Mitengo yaitalitali ‘nu
  • Hymn 839 Adani sindiopa mukalipo;
  • Hymn 261 Munafera pa mtanda
  • Hymn 1107 Anthu onse pansi pano
  • Hymn 1481 Timsankhe Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 652 Munene Mbuye ‘nenetu,
  • Hymn 985 Zonse zapadziko
  • Hymn 1851 Anthu onse, anthu onse,
  • Hymn 383 Zokoma ndi zakuyanja
  • Hymn 423 Koma azibvala
  • Hymn 1490 Musachitenso nthantha ‘yi,
  • Hymn 578 Falitsani mbiriyi,
  • Hymn 220 Kalekale ndinathawa,
  • Hymn 226 BWENZI ndinamkomanayo
  • Hymn 1086 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini moyo,
  • Hymn 107 MUBWERE kuno Mzimu ’Nu
  • Hymn 372 DZUŴA la Mulungu
  • Hymn 486 MPULUMUTSI Yesu,
  • Hymn 333 M’DZIKO lino tikhalamo
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 1094 Ambuye anachoka
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 494 Yesu, E, ndikufunani,
  • Hymn 1599 Inde, ndifuna kumvatu
  • Hymn 55 UNAKHETSEDWA mwazi do!
  • Hymn 1702 Pakufa ine Mbuye
  • Hymn 1222 Bwenzi ndimamkomanayo
  • Hymn 1757 Udzadziwitsa anthu
  • Hymn 318 TINALI ambiri ife,
  • Hymn 277 GWIRA zintchito zako,
  • Hymn 1507 Ndikampempha anditenge,
  • Hymn 398 Lero lino mwatipatsa
  • Hymn 909 Ife tikondwera, ife tikondwera,
  • Hymn 1206 Ndidzakukondani
  • Hymn 3 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 382 Mwadzoza mutu wanga ndi
  • Hymn 137 UTHENGA wa Ambuye
  • Hymn 1668 Kumdziwitsa ndiko moyo,
  • Hymn 1785 Tiyeni tizipita kwathu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version