Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 228 MWAKHULUPIRIRADI

  1. Home   »  
  2. Hymn 228 MWAKHULUPIRIRADI

Hymn 228 MWAKHULUPIRIRADI

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 228 MWAKHULUPIRIRADI

 

MWAKHULUPIRIRADI
Yesu Ambuyathu;
Muli nazo zakezo,
Zidzatu zinanso.
Mlungu wachisomocho
Mbuye wathu ndiye,
Ati zinthu zonsezo
Nzathu mwa Iyeyo.

(Zina ndi zinanzo
Zidza kwa ifedi,
Inde mtima wakewo
Uli wokomadi.)

Mwamva Yesu m’mtimamo,
Adzanso kaŵiri,
M’mene ali nanutu
Muli ndi Chimwemwe.
Ntchito zachifundozi
Iye watha izi,
Kuti mwawo m’Mwambamo
Naye tikhalebe.

Mwamva Mzimu wakewo,
Zake zimvekanso
Kugwa ngati mvulayo
Yachisomo chake.
Mzimu ndiye mphamvudi
M’moyo mwathu muno,
Mpaka tidzafikako
Komwe kuli Yesu

Post navigation

Previous: Hymn 227 NDIM’KONDE Kristuyo,
Next: Hymn 229 POYAMBAPO ndakondwadi.

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 471 Mbuye, tili ana anu,
  • Hymn 815 Dzuwa lapita,
  • Hymn 133 NSEMBE yake ya Kaini,
  • Hymn 381 Chakudya changa chabwino
  • Hymn 258 Kazembe wanga m’matenda,
  • Hymn 294 Yesu anali khanda
  • Hymn 730 A! Yesu mwapangana
  • Hymn 473 Mzinda woyerawo!
  • Hymn 231 Mwazi wa Yesu wokondwa
  • Hymn 105 Tiyamike Mbuye Yesu
  • Hymn 1109 Pamene ndisauka,
  • Hymn 1025 Ndikamayenda m’mdimamo,
  • Hymn 1356 Lemekeza Mlungu ‘Tate,
  • Hymn 1086 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini moyo,
  • Hymn 1080 Ambuye mundisunge
  • Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika,
  • Hymn 59 Tinachoka munjira ya imfa,
  • Hymn 77 MMENE Yesu adzabwera,
  • Hymn 1329 M’tali mutali m’phirimo
  • Hymn 367 Nonse okhala pansipa,
  • Hymn 184 LEKANI kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 1541 Tionetseni tonsetu
  • Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 1430 Ndipo pakulowa
  • Hymn 883 Pokupempherani
  • Hymn 519 Mverani, aimba anawo,
  • Hymn 84 Aleluya, Aleluya,
  • Hymn 556 Ndani pachimpandocho
  • Hymn 710 Nthano ya Hananiyayo
  • Hymn 1069 Zochimwa zathu m’mtimamo
  • Hymn 1555 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 983 Nkhondo ya Satana
  • Hymn 220 MULUNGU mundichitire chifundo,
  • Hymn 683 Musamaopa kanthu ‘yi, tamani Yesuyo;
  • Hymn 500 Mbuye Yesu andisunga
  • Hymn 1124 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 368 MULUNGU wanga, Dzuŵatu
  • Hymn 239 Akumwambawo
  • Hymn 312 Atate, mupatse zomwe tapemphazi,
  • Hymn 64 Mantha, nkhawa, ndi chisoni
  • Hymn 140 NDINAMIRA m’machimo, wosaonekanso,
  • Hymn 1594 Chikondano chakechi
  • Hymn 1627 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 376 PAMTANDA Mbuye anafera,
  • Hymn 1708 Pakugomedwapo
  • Hymn 981 Tiyeni Akristu,
  • Hymn 1152 Pokonda Yesuyo, mtendere!
  • Hymn 191 AMBIRI tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 417 M’BWERE Mlungu Mbuye wathu,
  • Hymn 319 NDIDZATANI ine,
  • Hymn 607 Dziko lonse lilikukondwa, mlengalenga mpheponso,
  • Hymn 212 NDI MISOZI, ndi chisoni,
  • Hymn 83 MBUYEYO adzabwera,
  • Hymn 1710 Pamtandapo, pamtandapo
  • Hymn 864 Ndi chikondi mtithandize kuigwira nkhondoyi;
  • Hymn 1559 Wotsogolera, munditsogolere
  • Hymn 194 Kuli dziko labwino m’Mwamba
  • Hymn 61 A! MUTU wakuyera,
  • Hymn 1750 Ndi nyali yakuwalitsa

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version