Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu, Mutidziwitse ‘Tate wathu, Ndi Mwana wake ndinu Mmodzi; Mnafuma kwa awiri onse, Koma Mulungu Mmodziyo.