Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu, Mutidziwitse ‘Tate wathu, Ndi Mwana wake ndinu Mmodzi; Mnafuma kwa awiri onse, Koma Mulungu Mmodziyo.