Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,

  1. Home   »  
  2. Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,

Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,

 

MLENGI wathu Woyeranu,
Mutimvere ‘fe;
M’wasungire akutali,
Bwinodi.

Mbuye Yesu,
m’yandikire,
M’wakondwetsebe;
Mulimbitse mphamvu zawo,
Zonsezo.

Akawona masautso,
M’khale nawodi;
Akondwere mwachikondi,
Chanucho.

Mpulumutsi wakukoma,
Muwagwirize;
Nsiku zonse akulemekezeni,
(Akule-mekezeni.)

Mzimu wanu Woyerawo,
Awayeretse;
Agonjetse ndi chisomo,
M’nkhondoyi.

Tate, Mwana, Mzimu, ndi ‘Nu,
Mlungu mmodzitu;
Muwasunge mfupi mwanu,
Ponsepo.

Post navigation

Previous: Hymn 448 CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,
Next: Hymn 450 YESU, munditsogoza

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 632 Tsopano tipereka mapemphero athu ano,
  • Hymn 97 Maso ndi maso ndi Kristu,
  • Hymn 1754 Ndiye akumbukira
  • Hymn 579 Pochezera m’dambomo,
  • Hymn 384 USIKU uja kalero,
  • Hymn 181 Zonse ndinakonda kale
  • Hymn 1558 Wosangalatsa, ine ndikalira
  • Hymn 1661 Ndimachitira
  • Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo
  • Hymn 201 NDILINKUDZA kwa Ambuye,
  • Hymn 501 Yesu andikonda ine;
  • Hymn 1583 Dzina la Yesuyo
  • Hymn 19 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 831 Mundikumbutse, ndikapanda tulo, za Kumwambako;
  • Hymn 300 AKRISTU limbikani,
  • Hymn 215 Choka, choka,
  • Hymn 572 Anadza nazo mphatso zake
  • Hymn 135 USANABADWE, Yeremiya,
  • Hymn 181 PANALITU wakudwala
  • Hymn 1043 Mbiri yake ubukitse,
  • Hymn 812 Ndi ena sanamvera ‘yi,
  • Hymn 230 AMBUYANGA Yesu,
  • Hymn 1463 Zoipa zakhululukidwa,
  • Hymn 470 YESU andikonda ine,
  • Hymn 215 TATE ndili mwana wanu,
  • Hymn 750 Yesu Mbuyathu, Inu nomwe ‘Nu,
  • Hymn 1790 Imfa ya anthu ake imkomera,
  • Hymn 125 ODALA ali iwo,
  • Hymn 965 Mundiuze, aulendo,
  • Hymn 63 POKUMBUKIRA mtandawo
  • Hymn 445 TILIMALIMA m’minda,
  • Hymn 505 Ndikondwa kuti Atate wam’Mwamba
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 341 Ayenda,
  • Hymn 1702 Pakufa ine Mbuye
  • Hymn 1114 Akukumbukira
  • Hymn 1782 Poyamba paja analenga
  • Hymn 250 MBUYANGA Yesu,
  • Hymn 1 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 63 Ndili nawo moyo w’satha
  • Hymn 289 Ndi manja athu awa nawo nganu,
  • Hymn 1428 Penyetsetsa Yesu
  • Hymn 3 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 220 Kalekale ndinathawa,
  • Hymn 55 Ambiri tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 702 Mbuye wathu mutipatsa
  • Hymn 464 Yesu atiuza tiyambemo,
  • Hymn 1543 Idzani, Mzimu Inu,
  • Hymn 1728 Zofuna zanga zonsezo
  • Hymn 392 Chimwemwe chomwe mpatseko
  • Hymn 535 Mbuye timlemekeze,
  • Hymn 514 Osanatu, osana,
  • Hymn 788 Moyo watsopano
  • Hymn 612 Oyamika Mlungu mbwere,
  • Hymn 1556 Mzimu Woyera, mudzetu kwa ine,
  • Hymn 679 Zipata zachitsulo zitseguke zonse mbee!
  • Hymn 506 Ndikondwa kuti Yesu akonda,
  • Hymn 1803 Nowayo nayendamo,
  • Hymn 1339 Musaope pokumbuka

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version