Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 335 KWATHU sipadziko, ndingopitilira,

  1. Home   »  
  2. Hymn 335 KWATHU sipadziko, ndingopitilira,

Hymn 335 KWATHU sipadziko, ndingopitilira,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 335 KWATHU sipadziko, ndingopitilira,

 

KWATHU sipadziko, ndingopitilira,
Ndadzikundikira chuma Kumwambako;
Mngelo akodola pakhomo la M’mwamba,
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.

Mbuye, ndi ‘Nu Bwenzi langa ndithu.
Ndichitenji ngati Kumwamba sikwathu?
Mngelo akodola pakhomo la M’mwamba,
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.

Andiyembekeza, chinthuchi ndidziwa,
Mpulumutsi wanga wandikhu’lukira;
Adzandipyoletsa pamene ndafoka,
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.

Mbuye watsogola ku Ulemerero,
Ndifuna kugwira dzanja lake konko;
Andidikiranso pakhomo la M’mwamba,
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.

Mu Ulemelero tidzakhala m’yaya,
Oyera mtimawo ali kulambira;
Ati: “Aleluya kwa Mlungu wamphamvu,”
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu

Post navigation

Previous: Hymn 334 KULI dziko labwino M’mwamba,
Next: Hymn 336 KULINSO dziko lowala M’mwamba,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 320 NDIKONDA Mlungu pomva Mbuye wanga
  • Hymn 490 YESU adza kuwerenga,
  • Hymn 333 Perekani, perekani
  • Hymn 1421 Alongo ‘nu, alongo ‘nu,
  • Hymn 136 MKAZI wa ku Samariya,
  • Hymn 1099 Sindidziwatu zamawa,
  • Hymn 804 Muchotse zonse zoti bii
  • Hymn 186 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 1807 Chithawa m’talitali
  • Hymn 1477 Anena anthu onsewo,
  • Hymn 317 Zambiri zagona m’kholamo,
  • Hymn 1407 Tula mtolo wako
  • Hymn 496 MBUYE dalitsani Afirika.
  • Hymn 1856 Mzimu, msandipitirire,
  • Hymn 998 Anatilemba Yesu tikagwire nkhondo yake,
  • Hymn 91 Ufuna kuyera kopambana?
  • Hymn 1611 Nadzuka m’mandamo
  • Hymn 975 Tiyeni, Akristu inu,
  • Hymn 1235 Yesu wathadi
  • Hymn 1113 Mtima wa Mbuyako
  • Hymn 587 Mutitsuke,
  • Hymn 1661 Ndimachitira
  • Hymn 992 Mukandipweteka,
  • Hymn 1471 Ukapenya kwa Yesu uliko moyoko,
  • Hymn 502 Ndikonda mbiri yomwe
  • Hymn 425 AKRISTU ndi abale, tiziyenderana tonse,
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 146 KODI ulikulemedwa
  • Hymn 430 Tero tidzakwera
  • Hymn 482 TCHIMO musalole, musadziipitse,
  • Hymn 324 Walira Yesu pazobvutazo,
  • Hymn 1474 Zilepheradi zonse kugula moyowo,
  • Hymn 257 NJIRA yanga sindiziŵa,
  • Hymn 1437 Yesu ndi wokonda;
  • Hymn 295 AMBUYE wa Kumwamba,
  • Hymn 1736 “Senzani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 920 Yatha misoziyo,
  • Hymn 98 Ndidzamwona maso ndi maso
  • Hymn 71 DZIKO lino lapansi, ndilibetu abwenzi,
  • Hymn 1139 Namondwe akawombabe,
  • Hymn 1145 Khalani duu! Mulungu wanuyu
  • Hymn 1768 Ndiye wamphamvu zonse
  • Hymn 821 Aleluya!
  • Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee!
  • Hymn 296 Mngelo anatumidwa
  • Hymn 1389 Tithawire kwa Mulungu,
  • Hymn 1264 Chifuniro change, Mbuye, Ndiperekachi;
  • Hymn 883 Pokupempherani
  • Hymn 395 Usiku uno mutisungedi,
  • Hymn 362 Imvani Yesu akuti:
  • Hymn 769 Ndi kutsukidwa m’mwazimo
  • Hymn 11 NDI mitima yokondwera,
  • Hymn 390 A! YESU, ndapangana
  • Hymn 694 Sadalekeza kuyamika
  • Hymn 777 Mulungu ali muno,
  • Hymn 1269 Ndifoka ndi zoipazo,
  • Hymn 1286 E, ndikukhulupirani,
  • Hymn 1357 Mlemekeze, anakonda
  • Hymn 127 Mwazi wake ndi chitsime changa,
  • Hymn 1850 Anthu a mitundu yonse,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version