Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

  1. Home   »  
  2. Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

 

NDILIKUMVA m’mtima mwanga
Mau ake a MbuyAnga,
Ati, “Ndakukonda iwe,
Kodi undikonda Ine?”

Ati; “Mwana, kumbukira
Zonse ndinakuchitira;
Ndakukonda, ndakufera,
Ndakufuna posokera.

“Ku zoipa zonse zako,
Goli la pakhosi pako,
Ndi kunthenda zosautsa
Ndine ndakupulumutsa

“Kodi mayi wobereka
Mwana wake adzamleka
Pena adzamwiŵalira,
Koma ndikukumbukira.

“Nthaŵi ilikudza yonse
Sindisinthanika konse;
Imfa sindiletsa Ine
Ndisakondekonde iwe.

“Ine ndidzakuonetsa
Zonse zakukondweretsa
Za Kumwamba zanga izo,
Mwana, sundikonda ine?”

Ambuyanga, ndalephera,
Mwachisoni ndipemphera
Mundipatse ine ndithu
Mtima wakukonda Inu.

Post navigation

Previous: Hymn 221 A! CHIKONDI chopambana,
Next: Hymn 223 ATI Yesu Mbuyeyo:

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 670 Isaleke ntchito yake
  • Hymn 651 Ikhale ngati nyali
  • Hymn 336 Perekani mtima wanu
  • Hymn 1203 Zambiri zangazo
  • Hymn 445 TILIMALIMA m’minda,
  • Hymn 962 Inde Mbuye, tibweradi,
  • Hymn 1341 Tadza kukudyaku,
  • Hymn 428 MBUYE mtsitsimutse
  • Hymn 1090 Chitsime chakuyera ine
  • Hymn 557 Usikuwo woyerawo!
  • Hymn 327 Yesu salephera ‘yi.
  • Hymn 819 Lero tigone,
  • Hymn 473 Mzinda woyerawo!
  • Hymn 802 Ndife anthu aulendo,
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 122 KUNALI munthu wa Mlungu,
  • Hymn 9 TAMANI Ambuye,
  • Hymn 77 Ndipereka zanga zonse,
  • Hymn 262 Tumphatumpha moyo wanga,
  • Hymn 65 NLA Mlungu dzuŵali:
  • Hymn 1393 Nditamatu Ambuyangayu,
  • Hymn 52 Mbwere Mzimu, mbwere!
  • Hymn 1319 Ambuye naitana ‘ne:
  • Hymn 147 MUSAŴALOLE mawuwo
  • Hymn 1299 Mzimu mndipatseko,
  • Hymn 66 >ALELUYA, Aleluya, Aleluya!
  • Hymn 118 PANALI munthu amene,
  • Hymn 414 INU bambo, inu mayi,
  • Hymn 64 LERO Kristu anauka,
  • Hymn 1295 Ambuye, mwazi wanuwo
  • Hymn 63 POKUMBUKIRA mtandawo
  • Hymn 1842 Pabande lolunjika andilondolera njira;
  • Hymn 95 Palibe mmodzi akanatha
  • Hymn 171 IWE tiye, iwe tiye,
  • Hymn 1309 Ndi inetu ndidziwedi
  • Hymn 1735 “Sezani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 395 Usiku uno mutisungedi,
  • Hymn 296 TIYENI Akhristu,
  • Hymn 421 ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,
  • Hymn 479 Munanena mulandira
  • Hymn 136 MKAZI wa ku Samariya,
  • Hymn 1497 Simbani mobwereza,
  • Hymn 419 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 1789 Nditani ine kubwezera Mbuye
  • Hymn 1669 Ukafuna kumdziwitsa,
  • Hymn 62 AMBUYE Yesu,
  • Hymn 1209 Mnyamata wake ndinetu,
  • Hymn 981 Tiyeni Akristu,
  • Hymn 1630 Anthu anu amafoka,
  • Hymn 27 LEMEKEZANI Yehova,
  • Hymn 335 Mtembenuke mtima wanu,
  • Hymn 1008 Wakuchezacheza naye
  • Hymn 888 Polowa ndi Inu
  • Hymn 1254 Mukhululukire ine,
  • Hymn 341 Ayenda,
  • Hymn 138 Kumva ulikumva, ulikumva,
  • Hymn 67 PAMENEPO pokhala madzulo,
  • Hymn 463 Yesu atiuza tiwale ‘fe,
  • Hymn 1152 Pokonda Yesuyo, mtendere!
  • Hymn 528 Amithenga ‘naimba pamlengapo,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version