Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 446 YAMIKANI nonse ’nu,

  1. Home   »  
  2. Hymn 446 YAMIKANI nonse ’nu,

Hymn 446 YAMIKANI nonse ’nu,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 446 YAMIKANI nonse ’nu,

 

YAMIKANI nonse ’nu,
Pomwimbira nyimbozi
Za masika athuwa;
Potumiza mvulayi,
Mlungu wathu yemwedi
Atipatsa zonsezi;
Timwimbire m’nyumbayi
Za masika athuwa.

Dziko lathu lonseli
Nla Mulungu yemweyu;
Atumiza mphatsozi
Zakutilimbitsadi,
Mmera wathu wonsewu,
Mbewu zathu zonsezi;
Timtamande Mbuyeyu
Wotipatsa zonsezi.

Nthaŵi yina Mbuyeyu
Adzafika pansipa,
Nadzakonza zonsetu;
Zosakondweretsazi
Naziponya m’motowo,
Koma m’nkhokwe mwakemo
Mudzadzala mbewu tho!
Zokomera bwinotu.

’Dzani Mbuye msangatu,
Msonkhanitse zonse phe;
Anthu anu onsewa,
Muwapulumutse ’wo
Zopweteka zawozo,
Ziwathera zonse phe!
’Dzani mu Ufumu ndi,
K’wasonkhanitsa onse.

Post navigation

Previous: Hymn 445 TILIMALIMA m’minda,
Next: Hymn 447 OYAMIKA Mlungu m’bwere,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1145 Khalani duu! Mulungu wanuyu
  • Hymn 925 Kodi umadandaula:
  • Hymn 1364 Uzani zamphamvu,
  • Hymn 1270 Ndayesa kudzikonzadi,
  • Hymn 158 Mzimu, mlonge m’mtimamo
  • Hymn 1474 Zilepheradi zonse kugula moyowo,
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 362 MUKHALE ndine, dzuŵalo laloŵa,
  • Hymn 34 Yesu Mbuyetu, mwafera
  • Hymn 753 Getsemane ndionako
  • Hymn 87 Aleluya, mwandigula,
  • Hymn 286 Atate, tifika pamaso panu;
  • Hymn 1295 Ambuye, mwazi wanuwo
  • Hymn 578 Falitsani mbiriyi,
  • Hymn 1046 Ndiyere mbuu! E, ndiyere mbuu!
  • Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;
  • Hymn 155 Pemphero ndiko kufuna
  • Hymn 1262 Lero mtima ungolema, Usaukadi;
  • Hymn 374 Pakuti Mfumuyo
  • Hymn 1421 Alongo ‘nu, alongo ‘nu,
  • Hymn 909 Ife tikondwera, ife tikondwera,
  • Hymn 69 Kwathu sipadziko, ndingopitirira,
  • Hymn 1105 Khala chete mtima wanga
  • Hymn 1497 Simbani mobwereza,
  • Hymn 413 Yesu ndiye Bwenzi lathu,
  • Hymn 1550 Kutiyeretsa m’mtima
  • Hymn 106 Ife, tapulumukadi,
  • Hymn 1640 Alinkudza Ambuye Yesu
  • Hymn 1515 Ndikachimwa, Bukuli
  • Hymn 246 Pajapo ndipenya
  • Hymn 695 Pomveka konsekonse mbiri
  • Hymn 149 Ndisauka, sindikhoza
  • Hymn 112 Pangano lake m’mwaziwo
  • Hymn 584 Ndi angelo,
  • Hymn 37 YESU analikhanda
  • Hymn 385 SINDILI woyenera ’ne,
  • Hymn 285 Ndipempha, Ambuye,
  • Hymn 295 AMBUYE wa Kumwamba,
  • Hymn 197 Tidzatama Atate wathu
  • Hymn 1605 Yesu, dzina lokondwetsa
  • Hymn 16 MTIMA wanga lemekeza,
  • Hymn 815 Dzuwa lapita,
  • Hymn 758 Sindili woyenera ‘ne;
  • Hymn 1258 Zonse zina sizikwana,
  • Hymn 195 Bwinoli tipita,
  • Hymn 332 NDIKONDWA kuganizirabe
  • Hymn 726 Mundidzze ndi chikondi,
  • Hymn 363 ATATE ndiyamika,
  • Hymn 1077 Khalatu woyera,
  • Hymn 1857 Ndinagona mwa zoipa,
  • Hymn 1829 Mulungu ndiye Mbusa wanga, sindisowa konse;
  • Hymn 189 Koma Iye wandipeza;
  • Hymn 557 Usikuwo woyerawo!
  • Hymn 1248 ‘Dzanitu Wamphamvu yonse,
  • Hymn 254 PAMENE ndisawuka,
  • Hymn 268 POKHALA mtendere mu mtimangamu,
  • Hymn 284 MAVUTO ndi ambiri,
  • Hymn 274 E! tidzakomanansotu
  • Hymn 13 Mtiwerengere m’Mwamba ndi oyera;
  • Hymn 575 Taonani m’kholamo

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version