Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 254 PAMENE ndisawuka,

  1. Home   »  
  2. Hymn 254 PAMENE ndisawuka,

Hymn 254 PAMENE ndisawuka,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 254 PAMENE ndisawuka,

 

PAMENE ndisawuka,
Pamene ndivutidwa;
Mizimu yakuipa,
Ikadza nindiyesa.

Mulungu wanga,
Mwini mphamvu;
M’kandikumbukire ‘ne.

Pamene ndilemedwa,
Ndi zakuipa zanga;
Polowa mdima m’mtima,
Pochita ine mantha.

Masiku anga onse,
Mulungu mundisunge;
Pamene ndimwalira,
Ndi tsiku lomaliza.

Post navigation

Previous: Hymn 253 YESU ndinutu wanga m’njira zonse,
Next: Hymn 255 KHALA chete mtima wanga

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1021 Kunsi kudambo, pena m’mwamba m’phirimo,
  • Hymn 596 Mlungu ali nane;
  • Hymn 263 Mulungu wakwezekatu,
  • Hymn 192 ZAKEYU mkulu wa misonkho,
  • Hymn 1070 Mthandize Mbuye, timvetu,
  • Hymn 16 Chikhulupiriro chathu
  • Hymn 993 Pakumalizidwa
  • Hymn 1643 Kufuna inetu, kufuna inetu,
  • Hymn 356 Tinafena m’nyanjamo,
  • Hymn 88 Ufuna kuwomboledwa kodi?
  • Hymn 618 ‘Dzani Mbuye msangatu,
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 1766 Ndilikulemekeza
  • Hymn 144 AMENE adzavomereza ndithu,
  • Hymn 799 Inu Mlungu kalelo
  • Hymn 1360 Ndi Aleluya imbirani
  • Hymn 326 TSIKU Iidzafika mbale,
  • Hymn 1603 Zina za Yesu m;Mwambamo,
  • Hymn 1048 Kumwamba ndiona Ambuyangayo,
  • Hymn 726 Mundidzze ndi chikondi,
  • Hymn 53 Dalitsani mafumu athu,
  • Hymn 1657 Mbuye, mutsaganebe
  • Hymn 1350 Mvera Yesu, mvera Yesu,
  • Hymn 27 LEMEKEZANI Yehova,
  • Hymn 193 A! Kumwamba
  • Hymn 1320 Ndayang’anira Mbuyeyo,
  • Hymn 1298 Ndikhulupira ‘Nu,
  • Hymn 101 Lodala tsiku lomwelo
  • Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,
  • Hymn 859 Pakufika tsidya lija,
  • Hymn 974 Tsopano timenyana
  • Hymn 1837 Mbuye ndiye wachifundo,
  • Hymn 189 Koma Iye wandipeza;
  • Hymn 120 Lekani kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 1622 Anthu onse amlambire
  • Hymn 1475 Anathera pamtanda zintchito zonsezi
  • Hymn 905 Iwo asekera, iwo asekera,
  • Hymn 87 Aleluya, mwandigula,
  • Hymn 1774 Poti akumbukira
  • Hymn 552 Analira ndaniyo
  • Hymn 608 Maluwa abwino aphuka m’mapiri ndi m’madambomo,
  • Hymn 22 MU ZONSE abale yamikani,
  • Hymn 778 Mwini madalitso,
  • Hymn 1155 Abale angakhale m’talimo
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 1632 Ndi chiyembekezo ichi
  • Hymn 736 Mndidyetse m’chipululu
  • Hymn 1007 M’mene umauka m’mawa,
  • Hymn 138 SANGALATSA akusowa, masiku alikutha,
  • Hymn 1506 Ndikamfunafuna Iye,
  • Hymn 1175 Sindinanyengedwa konse,
  • Hymn 1420 Abale ‘nu, abale ‘nu,
  • Hymn 1180 Ndine kapolo wa Mbuye wanga;
  • Hymn 836 Kamoyo kanga katha lero lino,
  • Hymn 350 Yesu ati,
  • Hymn 1806 Nowayo anatuma,
  • Hymn 757 Sindili woyenera ‘ne;
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 63 Ndili nawo moyo w’satha
  • Hymn 1386 Ndi chifundo atipenya

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version