Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 436 YEHOVA Mlungu wathu,

  1. Home   »  
  2. Hymn 436 YEHOVA Mlungu wathu,

Hymn 436 YEHOVA Mlungu wathu,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 436 YEHOVA Mlungu wathu,

 

YEHOVA Mlungu wathu,
Amene mumapatsa
Zipatso za chikondi
Polenga anthu anu,
Mupatse awa ‘ŵiri
Mitima yokondwetsa,
Yofana m’munda muja
Munayendamo kale.

Mbuyathu wokondedwa,
Pokhala m’dziko muno
Munadza ku ukwati,
Naŵadalitsa onse;
Ukwatiwu mukonze,
Mukhale nafe pano;
Iwowa m’ŵadalitse
M’chifundo chanu chonse.

Ndi Mzimutu Woyera
Mufike nayo mphamvu,
Mukatsangane nawo
Akupangana omwe;
Mupatse ’wo chisomo
Chokometsetsa mtima;
Chikuletu chikondi
Chitsazo nchanu chomwe.

Mulungu mwa Atatu,
Atate, Mwana, Mzimu,
Tikhaletu wokondwa
Ndi Inu m’chiyanjano;
Titama Inu Mlungu,
Wokonda ife ndinu;
M’ulendo wathu wonse
Tiyende m’chikondano.

Post navigation

Previous: Hymn 435 ANAKWATIRA kale
Next: Hymn 437 MULUNGU wa Yakobo Inu, mdyetsa anthu anu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 225 NDIDZAIMBA za Mulungu,
  • Hymn 378 KWEZANI mitu yanuyo,
  • Hymn 234 IMFA ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 1185 Imfa ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 417 M’BWERE Mlungu Mbuye wathu,
  • Hymn 249 MBUYANGA Yesu, mundigwire
  • Hymn 121 Imbira!
  • Hymn 465 ANA a Yerusalemu
  • Hymn 756 Sindili woyenera ‘ne,
  • Hymn 1100 Inde wakukonda ndinu;
  • Hymn 421 Ine ndine mlendo
  • Hymn 418 M’manja Yesu wanga
  • Hymn 509 Ndikadzaona Ambuye Kumwamba,
  • Hymn 181 PANALITU wakudwala
  • Hymn 398 Lero lino mwatipatsa
  • Hymn 1114 Akukumbukira
  • Hymn 1554 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 1148 Ndiimba mumtima mokondwa
  • Hymn 59 IMVANI uthenga,
  • Hymn 612 Oyamika Mlungu mbwere,
  • Hymn 663 Anyamata a Mulungu,
  • Hymn 1046 Ndiyere mbuu! E, ndiyere mbuu!
  • Hymn 1856 Mzimu, msandipitirire,
  • Hymn 1629 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 1093 Odala ndi onsewo
  • Hymn 1701 Nditani Bwenzi langa
  • Hymn 1199 Ndikhumba ine ndithu
  • Hymn 37 Pozunzidwa inu ponseponsepo
  • Hymn 427 AULENDO amayenda
  • Hymn 339 MTIMA wanga ndikonzera,
  • Hymn 1300 Poyenda m’mdima bii,
  • Hymn 1239 Ndipo pakuima phe!
  • Hymn 443 Tchimo musalole,
  • Hymn 185 NDINE Mbusayo wabwino,
  • Hymn 1083 “Khala mwa Ine,” Yesu anatero;
  • Hymn 1777 Mulungu wamkulu
  • Hymn 62 AMBUYE Yesu,
  • Hymn 190 CHITETEZO chachikulu
  • Hymn 582 A! Mulungu,
  • Hymn 1156 Imfa ndi manda sitiopa ‘yi,
  • Hymn 1799 Mulungu atipatsa mphamvu
  • Hymn 452 MLUNGU, Inutu,
  • Hymn 215 TATE ndili mwana wanu,
  • Hymn 54 Dalitsani mafuko onse,
  • Hymn 7 NDI Aleluya imbirani,
  • Hymn 848 Mudze, mlowe m’mtimamu,
  • Hymn 276 Dziko lonse mlambire
  • Hymn 195 YESU wondikondadi,
  • Hymn 1478 Azizwa anthu ajawo,
  • Hymn 846 Kristu wakuyeratu,
  • Hymn 1679 Tiyamike Dzina lake, Aleluya,
  • Hymn 706 Tisaiwalire ‘bale
  • Hymn 29 CHIKONDI cha
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 675 Pamaiko pali mdima,
  • Hymn 1719 Ku Mzinda wakuyerawo
  • Hymn 169 ’MVANI liu lomwe
  • Hymn 279 Mbwere mudzamve nonse
  • Hymn 94 KHAMULO liliko

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version