Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 339 MTIMA wanga ndikonzera,

  1. Home   »  
  2. Hymn 339 MTIMA wanga ndikonzera,

Hymn 339 MTIMA wanga ndikonzera,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 339 MTIMA wanga ndikonzera,

 

MTIMA wanga ndikonzera,
Mbuye Yesu aitana;
Ati: “Mwana, tapemphera,
Ine sindidzakukana.”

Mbuye ndinu Mfumu yanga
Yolemera ndi yamphamvu;
Ndikapemphatu zambiri,
Simundimanira kanthu.

Ndikabwera nd katundu
Wa zoipa zanga zonse;
Mwazi wake wa Ambuye,
Udzandiyeretsa konse.

Mbuye ndinalema ine,
Mloŵe Inu m’mtima mwanga;
Mkhale m’mwemo mwini wake,
Mantha mwandichotsera ’ne.

Ndine mlendo pansi pano,
Mndilimbitse ndi chikondi;
Bwenzi mundilondolere
Njira pa ulendo wonse.

Mndidziŵitse ntchito yanga,
Mphamvu yake mundipatse;
Mundilimbikitse m’mtima
Ndikhale kwa Atate.

Post navigation

Previous: Hymn 338 ’TATE wa Kumwambako,
Next: Hymn 340 PEMPHERA m’mbanda kucha,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1536 Ndilira Mzimu leroli,
  • Hymn 197 Tidzatama Atate wathu
  • Hymn 906 Mulibe zoipa m’Dzikolo,
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 404 Dzuwa la lero lonseli
  • Hymn 352 Tiyamike Mlunguyo,
  • Hymn 46 O! ufulu tigwirizane
  • Hymn 1139 Namondwe akawombabe,
  • Hymn 31 Tamandani mbuye,
  • Hymn 610 Nafenso tidzadzuka kwa ‘ke ngati maluwawo,
  • Hymn 501 Yesu andikonda ine;
  • Hymn 361 AMBUYE munapatsa tsiku
  • Hymn 341 Ayenda,
  • Hymn 804 Muchotse zonse zoti bii
  • Hymn 1478 Azizwa anthu ajawo,
  • Hymn 1183 Adalitsika, indetu,
  • Hymn 1562 Mzimu Woyera, mudze mumitima mwathumo,
  • Hymn 1407 Tula mtolo wako
  • Hymn 50 Akhristu nyamulani
  • Hymn 91 NDITAME Mlungu m’mtimamo,
  • Hymn 1033 Mkristu gwiratu ntchito
  • Hymn 470 Mutiletse tisaname
  • Hymn 411 Yesu adza kukundika
  • Hymn 772 Muwalimbikitse onse
  • Hymn 272 Ankhondowo poona
  • Hymn 151 UKAPENYA kwa Yesu uliko moyoko,
  • Hymn 34 AMITHENGA a Mulungu,
  • Hymn 1 NDINU wakuyera! Wamphamvu zonse.
  • Hymn 1039 Usafune chuma chokha,
  • Hymn 593 Yesu, munditsogoza
  • Hymn 1806 Nowayo anatuma,
  • Hymn 909 Ife tikondwera, ife tikondwera,
  • Hymn 226 BWENZI ndinamkomanayo
  • Hymn 1086 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini moyo,
  • Hymn 705 Tikhaletu nawo, Mbuye,
  • Hymn 173 Mema nkhondoyo, wadza mdaniyo,
  • Hymn 1419 Amayi ‘nu, amayi ‘nu,
  • Hymn 57 Ife tiyembekezera Yesu,
  • Hymn 442 MASIKA a m’dziko Mbuye,
  • Hymn 1326 A! Mbusa wathu amvatu
  • Hymn 961 Mbuye anatiitana
  • Hymn 548 Kale anthu m’kholamo
  • Hymn 422 DZIKO lonse lapansi,
  • Hymn 1848 Tiyamike Mlungu wathu
  • Hymn 1772 Iye amakhutitsa
  • Hymn 834 Tiyamike Mlungu wotipatsa zachifundozi,
  • Hymn 1261 Kale ndinakana Inu, Ndinathawatu;
  • Hymn 57 TIYENI, dzalireni nane,
  • Hymn 1657 Mbuye, mutsaganebe
  • Hymn 1439 Iwetu afuna,
  • Hymn 275 NTHAWI yathu yafikatu,
  • Hymn 695 Pomveka konsekonse mbiri
  • Hymn 323 >APITA anzathu dzuŵa lino
  • Hymn 360 Muli ndi ludzu, idzani
  • Hymn 1130 Mbuyanga Yesu, mundigwire dzanja
  • Hymn 1165 Dzanja la Mulungu
  • Hymn 952 Ndimayenda paulendo,
  • Hymn 755 Pamene padzakhalapo
  • Hymn 880 Bwenzi lathu ndiye Yesu
  • Hymn 1576 Khamulo liliko

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version