Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

  1. Home   »  
  2. Hymn 390 A! YESU, ndapangana

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

 

A! YESU, ndapangana
Kutumikira ’Nu
Ndi moyo wanga wonse,
Mbuyanga ndinutu;
Mukhaletu pafupi
Masiku onsewo,
Sindidzaopa konse,
Mutsogolereko.

Ndikufuna kumva Inu,
E, Mawu anuwo,
Ndisamve za satana
Zonyenga zakezo;
Adani anga onse
Andizingiratu;
Mukhaletu pafupi,
Mundithangate ’Nu.

A! Yesu mwapangana
Ndi anthu anuwo
Adzakhala ndinu
Ku Dziko lanulo;
Inenso ndapangana
Ndisabwerere ’yi;
Mndipatse mphamvu yanu
Ambuye ndinudi.

Mundionetse, Yesu,
Mapazi anuwo,
Ndidzapondera awa
Munjira monsemo;
Ndithangateni ine
Ndisalefuke ’yi;
Mundilandire m’Mwamba
Ndikamwaliradi.

Post navigation

Previous: Hymn 389 NDIMAMVA njala, Yesu,
Next: Hymn 391 MUNDIMVERE, Mbuye wanga

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1693 Koma masauko ake Aleluya
  • Hymn 343 Auke,
  • Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
  • Hymn 790 Zimbalame zonsezi
  • Hymn 546 Kulibe wokwanira ‘yi
  • Hymn 171 IWE tiye, iwe tiye,
  • Hymn 297 POKUMANA m’mayesero a dziko lino,
  • Hymn 1 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 336 KULINSO dziko lowala M’mwamba,
  • Hymn 1343 M’dzina la Yesuyo
  • Hymn 352 Tiyamike Mlunguyo,
  • Hymn 791 Anthu opembedzawo
  • Hymn 510 Ngolizo zilira
  • Hymn 157 INU nonse ovutidwa,
  • Hymn 844 Pogona ife, amadzuka
  • Hymn 388 Ambuye, Mzimu wanu
  • Hymn 1158 Yesu ndiye Mbuye wanga,
  • Hymn 1368 Mitambo inu yakumwambako,
  • Hymn 1222 Bwenzi ndimamkomanayo
  • Hymn 1148 Ndiimba mumtima mokondwa
  • Hymn 297 Anapita nasiya
  • Hymn 1217 Chisoni chonsecho
  • Hymn 1814 Thupi lamwazi wathu’li
  • Hymn 1046 Ndiyere mbuu! E, ndiyere mbuu!
  • Hymn 783 Antchito a Mulungu ‘nu
  • Hymn 1782 Poyamba paja analenga
  • Hymn 785 Yehova adalitse ‘nu,
  • Hymn 1609 Idzani nose’nu
  • Hymn 1345 Iwe tiye, iwe tiye,
  • Hymn 1545 Mundilimbitse m’mtima
  • Hymn 440 Yesu wakufatsa mtima
  • Hymn 65 Chisomo chodabwitsacho
  • Hymn 1006 Yesu ati, “Ndidza msanga!”
  • Hymn 1020 Ngati umtsata Mpulumutsi wakoyo,
  • Hymn 800 Yesu munadzukanso
  • Hymn 1172 Adzabweranso
  • Hymn 64 LERO Kristu anauka,
  • Hymn 1254 Mukhululukire ine,
  • Hymn 764 “Chikho cha mwazi wangachi
  • Hymn 490 YESU adza kuwerenga,
  • Hymn 626 Inde, ‘Tate, mtiyendetse
  • Hymn 724 Ndine mlendo pansi pano,
  • Hymn 1016 Mbuye, mwatiuza ‘fe
  • Hymn 1541 Tionetseni tonsetu
  • Hymn 1214 Mwamva Mzimu wakewo,
  • Hymn 244 Ndidze pafupi pa
  • Hymn 318 Ambuye, muli nazo zambirizi,
  • Hymn 1399 Yesu ponong’oneza, idzanitu;
  • Hymn 1058 Chimwemwe chija chamumtima
  • Hymn 472 Amakumbukira zonse
  • Hymn 475 Mbuye ndikhaletu
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 898 Mndidziwitse ntchito yanga,
  • Hymn 992 Mukandipweteka,
  • Hymn 218 NDIPEREKA zanga zonse
  • Hymn 1039 Usafune chuma chokha,
  • Hymn 40 Padziko pano tikhalira
  • Hymn 1069 Zochimwa zathu m’mtimamo
  • Hymn 1096 Tifuna Inu, Mbuye,
  • Hymn 1331 Yesu wathu Mbuyeyo

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version