Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 364 DZUŴA lapitira,

  1. Home   »  
  2. Hymn 364 DZUŴA lapitira,

Hymn 364 DZUŴA lapitira,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 364 DZUŴA lapitira,

 

DZUŴA lapitira,
Wadza mdimawo,
Mthunzi wamadzulo
Wagwa m’mwambamo.

M’mwambamo nyenyezi
Zithwanima mbee;
Zonse zili m’tulo
Pansi pali duu.

Yesu mutipatse
Tulo toti phee;
Ndi mdalitso wanu
Mndigonetse ’ne

Mpatse ana ’ng’ono
Alotemo mbee;
Anthu aulendo
Msungesungebe.

Mutonthoze mtima
Wopwetekawo;
Akutsata tchimo
Mletse onsewo.

Wonsewu usiku
Andisunge ’ne
Amithenga anu
Akuyera mbee.

Ndidzukanso m’maŵa,
Kucha koti mbuu,
Ndiyeretu mtima
M’maso mwanumo.

Titamadi ’Tate,
Mwana wakeyo,
Mzimu Woyeranso,
Nthaŵinthaŵizo.

Post navigation

Previous: Hymn 363 ATATE ndiyamika,
Next: Hymn 365 DZUŴA lapita,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 366 Anthu onse a padziko
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu
  • Hymn 1623 Adzatenga anthu ake
  • Hymn 189 MLENDO ali pakhomo,
  • Hymn 596 Mlungu ali nane;
  • Hymn 360 Muli ndi ludzu, idzani
  • Hymn 300 Ona Mwanawankhosayo
  • Hymn 658 Ndichitireni, Mbuye ‘ne,
  • Hymn 765 Chikondi chili m’chikhomu
  • Hymn 20 CHIKONDI cha Mulungu wathu,
  • Hymn 775 Mwa anthu onsewo
  • Hymn 1545 Mundilimbitse m’mtima
  • Hymn 1473 Anasenza pa bwanji uchimo wonsewo,
  • Hymn 442 MASIKA a m’dziko Mbuye,
  • Hymn 278 Aweruza ndi mphamvu
  • Hymn 1046 Ndiyere mbuu! E, ndiyere mbuu!
  • Hymn 533 Ananu, ziimbani,
  • Hymn 150 Ndisauka, sindiona;
  • Hymn 1484 Idzatu, idzatu
  • Hymn 482 TCHIMO musalole, musadziipitse,
  • Hymn 250 Lidze msanga dzuwa lanu
  • Hymn 952 Ndimayenda paulendo,
  • Hymn 1511 Mndidalitsere ‘ne
  • Hymn 1584 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 1608 Yesu, dzina lakukonda
  • Hymn 146 Inu ndidzatama
  • Hymn 1122 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine
  • Hymn 595 Mbuye, ndinu wamphamvu,
  • Hymn 773 Mtsinje woyerawo
  • Hymn 221 A! CHIKONDI chopambana,
  • Hymn 426 MBUYE, Mpingo wanu usauka kwakukuludi;
  • Hymn 806 Kapena wina leroli
  • Hymn 83 Mpulumutsi Wokondedwa,
  • Hymn 1113 Mtima wa Mbuyako
  • Hymn 188 Ine ndili ndi manyazi
  • Hymn 1519 M’Buku lakuyerali
  • Hymn 1172 Adzabweranso
  • Hymn 541 Ana inu, yamikani
  • Hymn 388 Ambuye, Mzimu wanu
  • Hymn 821 Aleluya!
  • Hymn 889 Pemphera m’mbanda kucha,
  • Hymn 457 Palibe mwana wakuchepa
  • Hymn 5 Inu Mulungu, tikuyamikani;
  • Hymn 1514 Dzinthu zakumundazo
  • Hymn 75 Ndiperekatu
  • Hymn 323 >APITA anzathu dzuŵa lino
  • Hymn 183 Mlemekeze, bukitsani,
  • Hymn 1426 Wina panalibe
  • Hymn 216 NDISAUKA, ndinachimwa,
  • Hymn 370 KWACHA lero kwati mbee,
  • Hymn 467 Ife ana sitiopa,
  • Hymn 1660 Ndikakhumudwa
  • Hymn 1117 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 705 Tikhaletu nawo, Mbuye,
  • Hymn 184 LEKANI kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 277 Mbwere nonse muone
  • Hymn 1542 Titamire nthawi zonse
  • Hymn 33 OWONADI mtima,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version