Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 308 AULENDO, munka kuti

  1. Home   »  
  2. Hymn 308 AULENDO, munka kuti

Hymn 308 AULENDO, munka kuti

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 308 AULENDO, munka kuti

 

AULENDO, munka kuti
Ndi zindodo m’manja mwanu?
Paulendo tizipita;
Aitana Mbuye wathu;
Pamapiri, pamadambo
Tizipita komwe kwawo.
Tizipita komwe kwawo
Kuli dzikolo labwino,
Tizipita komwe kwawo
Kuli dzikolo labwino.

Kodi simuopa njira,
Inu anthu akufoka?
Ayi, atiperekeza
Mbuye wathu wotikonda.
Iye amakhala nafe,
Natitsogolera ife.
Atitsogolera ife
Kuli dzikolo labwino.
Atitsogolera ife
Kuli dzikolo labwino.

Mundiuze, aulendo,
Muli chiani m’Mwamba muja?
Atibvekako zoyera
Akorona natininkha;
Moyo, moyo atipatsa,
Kwa Mulungu tidzakhala.
Kwa Mulungu tidzakhala
Kuli dzikolo labwino,
Kwa Mulungu tidzakhala
Kuli dzikolo labwino.

Kodi inu, aulendo,
Ife titsagane nanu?
Inde, mudze inu nonse,
Mudze nafe paulendo.
Inde, mutiperekeze,
Yesu atilinda ife.
Yesu atilinda ife
Kuli dzikolo labwino,
Yesu atilinda ife
Kuli dzikolo labwino.

Post navigation

Previous: Hymn 307 ABALE anga ine ndikupita,
Next: Hymn 309 ANA akumwamba ndife,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 592 Kuti m’Mwambamo
  • Hymn 82 YANG’ANANI, anthu onse,
  • Hymn 483 Ndife akuchoka,
  • Hymn 619 Tilimalima m’minda,
  • Hymn 620 Mphatso zonse zathu
  • Hymn 618 ‘Dzani Mbuye msangatu,
  • Hymn 1404 “Undipatsetu
  • Hymn 116 Nkhosa zanga zimandimva
  • Hymn 1182 Chikhulupiro chomwenso
  • Hymn 1171 Mulungu wanga
  • Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo
  • Hymn 786 Yesu mkhale nafe
  • Hymn 69 Kwathu sipadziko, ndingopitirira,
  • Hymn 658 Ndichitireni, Mbuye ‘ne,
  • Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
  • Hymn 1034 Mkristu, ulimbike
  • Hymn 1269 Ndifoka ndi zoipazo,
  • Hymn 410 MAWU akewo anamveka ponse,
  • Hymn 233 M’mene ndapenya mwazi wa
  • Hymn 1761 Amithenga anaimba
  • Hymn 475 Mbuye ndikhaletu
  • Hymn 1639 Aleluya, aleluya,
  • Hymn 1168 Aleluya, muyenera!
  • Hymn 1571 Tamani mphamvu ya Yesu,
  • Hymn 63 Ndili nawo moyo w’satha
  • Hymn 760 Usiku uja kalelo
  • Hymn 318 TINALI ambiri ife,
  • Hymn 432 KRISTU ndiye Mwala wathu,
  • Hymn 17 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 481 Yesu wa Kumwamba,
  • Hymn 80 Utsegule mtimawo,
  • Hymn 479 ANYAMATA inutu,
  • Hymn 1559 Wotsogolera, munditsogolere
  • Hymn 491 KWA Yesu ndi kwabwinoko,
  • Hymn 1565 Mufike monga ngati njiwa yamtenderewo,
  • Hymn 463 Yesu atiuza tiwale ‘fe,
  • Hymn 1196 E! chikondi ndithu,
  • Hymn 1757 Udzadziwitsa anthu
  • Hymn 289 Ndi manja athu awa nawo nganu,
  • Hymn 806 Kapena wina leroli
  • Hymn 41 MKATI mwa zovuta zathu
  • Hymn 1321 Thanthwe long’ambikatu,
  • Hymn 422 Kwathu nkopambana,
  • Hymn 1653 Mulungu ali wokhulula mtimatu,
  • Hymn 476 Mpaka ndabvala mbuu!
  • Hymn 28 AMBUYE ngwodalitsika,
  • Hymn 149 Ndisauka, sindikhoza
  • Hymn 1712 E! Yesu Mbuye wangadi,
  • Hymn 167 KODI mwalandira Yesu?
  • Hymn 1427 Penyetsetsa Yesu,
  • Hymn 1835 Mtima wanga lemekeza
  • Hymn 623 Mbuye, tikuthokozani,
  • Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
  • Hymn 1622 Anthu onse amlambire
  • Hymn 470 Mutiletse tisaname
  • Hymn 140 NDINAMIRA m’machimo, wosaonekanso,
  • Hymn 304 POZUNZIDWA inu ponseponse
  • Hymn 978 Mtima wanu wonse ndithu
  • Hymn 1606 Yesu, dzina lakufatsa,
  • Hymn 1519 M’Buku lakuyerali

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version