Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,

  1. Home   »  
  2. Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,

Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 306 YAMBA ulendo mnzanga,

 

YAMBA ulendo mnzanga,
Wopita Kumwamba;
Ulendo wopambanadi,
Woyenda ndi mtima.

Udzakondwerera,
Ukayenda naye;
Yesu Mtetezi,
Ndi Mulungu wanga.

Usazengereze ‘we,
Ulendo ngwabwino;
Lapadi machimo ako,
Yesu afuna ‘we.

Post navigation

Previous: Hymn 305 NDALIMVA dziko la m’talimo,
Next: Hymn 307 ABALE anga ine ndikupita,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 261 M’NDIYANDIKITSE nanu Yesu,
  • Hymn 1563 Mufike monga nyali younika m’mtimamo,
  • Hymn 70 Mbuye ndinu bwenzi langa ndithu,
  • Hymn 190 Nsiku zonse kwanja kwake
  • Hymn 727 Imfa ikandifikira,
  • Hymn 1801 Nafuna kwaononga
  • Hymn 238 Mbuye Yesu, lowani m’mtima,
  • Hymn 73 Mu ulemerero tidzakhala m’yaya,
  • Hymn 359 TADZUKA mzimu wanga ‘we,
  • Hymn 463 MNANDIDZERA, Ambuye,
  • Hymn 1012 Ndi zipatsozo,
  • Hymn 1420 Abale ‘nu, abale ‘nu,
  • Hymn 1530 Mndilimbitse ndipirire
  • Hymn 374 NDI lokoma m’Mwambamo,
  • Hymn 32 Tamandani Mbuye,
  • Hymn 246 NAMONDWE akawombabe,
  • Hymn 333 Perekani, perekani
  • Hymn 322 Walira Yesu m’dziko linoli,
  • Hymn 134 INU ansembe ngakhale mufunsa,
  • Hymn 275 Mlungu akuyang’aniredi,
  • Hymn 1027 Tithawiranji ifetu?
  • Hymn 228 MWAKHULUPIRIRADI
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 958 Ndikalowa m’mtsinje muja,
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 1513 M’Bukuli ine ndi
  • Hymn 1380 Tilemekezetu
  • Hymn 33 OWONADI mtima,
  • Hymn 651 Ikhale ngati nyali
  • Hymn 1288 Yesu mundimve, ndikuliratu,
  • Hymn 461 Inu nonse anzanga,
  • Hymn 1076 Khalatu woyera,
  • Hymn 1080 Ambuye mundisunge
  • Hymn 5 ATATE wa Kumwambako,
  • Hymn 1097 Njira yanga sindidziwa,
  • Hymn 1619 Adzabwera,
  • Hymn 1141 Pakulekana ifetu
  • Hymn 721 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 771 Tsopano alandira
  • Hymn 1660 Ndikakhumudwa
  • Hymn 788 Moyo watsopano
  • Hymn 1345 Iwe tiye, iwe tiye,
  • Hymn 749 Ndiye wodyetsa anthu omwewo,
  • Hymn 1580 Akadakhalabe
  • Hymn 1008 Wakuchezacheza naye
  • Hymn 392 Chimwemwe chomwe mpatseko
  • Hymn 204 NDASIYA zonse ndi Yesu kalelo,
  • Hymn 146 KODI ulikulemedwa
  • Hymn 141 TAONANI pamtandapo,
  • Hymn 890 Kumbuka ‘bale ako
  • Hymn 457 Palibe mwana wakuchepa
  • Hymn 1825 Zobvuta zoopsa ndi zosaukazi
  • Hymn 833 Mundilimbitse ndikayese manda ngati mphasayi,
  • Hymn 226 Nditama mwaziwo!
  • Hymn 11 NDI mitima yokondwera,
  • Hymn 381 Chakudya changa chabwino
  • Hymn 121 Imbira!
  • Hymn 158 Mzimu, mlonge m’mtimamo
  • Hymn 291 ULENDO wachikhrisitu ngosawutsa ndithu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version