Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

  1. Home   »  
  2. Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

 

KUNALI munthu ku Yeriko,
Dzina lake Zakeyu;
Anali munthu wamkulu,
Wokhometsa misonkho.

(M) Kunali Zakeyu,
(O) Ku Yeriko,
(M) Nafunafuna,
(O) Kuwona Yesu,
(M) Koma chifukwa,
(O) Cha khamulo,
Anakwera mumtengo.

Paulendowo Ambuyeyo,
Anafika pamtengo;
Nayang’ana m’mwamba muja,
Anawona Zakeyu,

Ambuye Yesu nanenadi,
“Fulumira nutsike;
Lero lino ndiyenera,
Kukhala m’nyumba mwako.”

Zakoyuyo mofulumira,
Anatsika mumtengo,
Anam’tenga Mbuye Yesu,
Kuti akam’chereze,

Anadandauladi ena,
“Ambuye wachitanji?
Bwanji Iye analowa,
M’nyumba ya wochimwayo?”

Zakeyuyo pakumva ichi,
Anawuza Ambuye:
“Theka la chuma changacho,
Ndidzapatsa osowa.”

Leronso chipulumutsochi,
Chagwera m’nyumba yathu;
Tilape zoipa zathu,
Kutí tipulumuke.

Post navigation

Previous: Hymn 213 INE ndili ndi manyazi
Next: Hymn 215 TATE ndili mwana wanu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 302 Anasenza m’thupi mwake;
  • Hymn 1625 Ife tonse tikumbuke
  • Hymn 564 Ndi chifukwa atikonda,
  • Hymn 955 Komwe ndi chimwemwe ine
  • Hymn 433 Zoipa ndi zabwino
  • Hymn 801 Lero mwatipatsa moyo,
  • Hymn 1838 Ndiye Mbuye wa ambuye;
  • Hymn 917 Ndi nkhondo ikaleka
  • Hymn 358 MLUNGU ali muno,
  • Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,
  • Hymn 1067 Ambuyathu, ndikhumba tsiku lija
  • Hymn 946 Ngakhale enawo aleke kwimbako,
  • Hymn 775 Mwa anthu onsewo
  • Hymn 101 Lodala tsiku lomwelo
  • Hymn 970 Pena kumwa nawo,
  • Hymn 470 Mutiletse tisaname
  • Hymn 718 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 411 TAMVA mawu omwewo,
  • Hymn 501 Yesu andikonda ine;
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 1553 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 1500 Simbani Mbiri yomwe,
  • Hymn 324 Walira Yesu pazobvutazo,
  • Hymn 316 NDAMVATU kuti tifika komweko
  • Hymn 237 SINDINANYENGEDWA konse
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,
  • Hymn 1557 M’phunzitsi, ndinu mudziwitse ine
  • Hymn 1539 Kudzoza kwa Kumwambako
  • Hymn 977 Musagonje, anthu inu,
  • Hymn 1602 M’mawu a Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 951 Ndi kale lonse mnandisunga ‘ne;
  • Hymn 1423 Oipa inu nonsetu,
  • Hymn 762 “Ndi thupi lopatsidwali
  • Hymn 1028 Yendani bwino m’njiramo
  • Hymn 608 Maluwa abwino aphuka m’mapiri ndi m’madambomo,
  • Hymn 611 Tidzakhala naye nthawi zonse ndi kuimbako,
  • Hymn 1454 Ambuye, musendeze
  • Hymn 1377 Ndi amithenga akumwambako,
  • Hymn 1810 Kalelo Mbuye Yesu
  • Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine
  • Hymn 108 Tikondwera ife tonse
  • Hymn 493 Ndimalira kwa Inutu,
  • Hymn 1641 Pakufika asonkhanitsa
  • Hymn 1712 E! Yesu Mbuye wangadi,
  • Hymn 781 Tatsegukani inutu,
  • Hymn 543 Kuli kaphiri m’talimo
  • Hymn 1485 Unachimwachimwa ndithu,
  • Hymn 293 LIMBA mtima mbale wanga
  • Hymn 1404 “Undipatsetu
  • Hymn 1747 Yesu aitana ife;
  • Hymn 545 Anatifera tonsefe
  • Hymn 912 Makomo afanana
  • Hymn 95 TAMANI mphamvu ya Yesu,
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 177 ŴALIRA Yesu m’dziko linoli,
  • Hymn 509 Ndikadzaona Ambuye Kumwamba,
  • Hymn 1102 Dziko lonse ndilitaya;
  • Hymn 1316 Ndabwera kwa Ambuyeyo:
  • Hymn 18 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 787 Mzimu Wakuyera

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version