Chichewa Christian Hymns
Hymn 20 CHIKONDI cha Mulungu wathu,
CHIKONDI cha Mulungu wathu,
Kutumiza Mwana wakeyo,
Kutifera ife tonse’fe,
Kutipulumutsa.
Kweza, kweza maso,
Kwa Atate.
Udzalandira moyo,
Wosathawo.
Mtima wanu usavutike,
Khulupilirani Mulungu;
Khulupilirani Inenso,
Mudzapulumuka.