Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 21 KUZANI Mlungu m’Mwambamo,

  1. Home   »  
  2. Hymn 21 KUZANI Mlungu m’Mwambamo,

Hymn 21 KUZANI Mlungu m’Mwambamo,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 21 KUZANI Mlungu m’Mwambamo,

 

KUZANI Mlungu m’Mwambamo,
Mtamande m’kuyanso;
Nzozizwa nkhani zakezo,
Njolimba ntchito njo!

Pochimwa anthu onsewo
Nja Mlungu nzeruyi;
Adamu wachiŵiriyo
Wathetsa tchimoli.

Thupi la mwazi wathu ’li
Lochimwa kalelo,
Labweranso ku nkhondoyi,
Laposa monsemo.

Choposa nalo thupilo
Chikhale momwemu,
Chiyeretsetsa m’katimo,
Ndi Mulungu Iyeyu.

Anatikondakonda ’Ye,
Ndi Mlungu Iyeyo,
Anatifera anthu ’fe
Ndi Mulungu Iyenso.

Ndi m’munda muja chete, phee!
Pamtanda pati njo!
Anaphunzitsa’bale ’fe
Titero ifenso.

Kuuzani Mlungu m’Mwambamo
Mtamande m’kuyanso;
Nzozizwa nkhani zakezo,
Njolimba ntchito njo!

Post navigation

Previous: Hymn 20 CHIKONDI cha Mulungu wathu,
Next: Hymn 22 MU ZONSE abale yamikani,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 130 Tidzakondweradi m’Mwambamo
  • Hymn 913 Kulibe gombe, nyanja,
  • Hymn 198 M’dziko lino tikhalamo
  • Hymn 1344 Yamba ulendowo
  • Hymn 1384 Mphamvu yake inalenga
  • Hymn 372 Potero onsewo
  • Hymn 491 KWA Yesu ndi kwabwinoko,
  • Hymn 148 Ndisauka, ndimasowa
  • Hymn 314 E, moto wanu woyera
  • Hymn 1643 Kufuna inetu, kufuna inetu,
  • Hymn 169 M’manda nagonamo
  • Hymn 839 Adani sindiopa mukalipo;
  • Hymn 1316 Ndabwera kwa Ambuyeyo:
  • Hymn 877 Zokoma ndithu nthawizi
  • Hymn 484 YESU ndiye Mbusa,
  • Hymn 1634 Pakwitana Mbuye wanga
  • Hymn 1644 Popachikidwa pa Golgotapo
  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 350 Yesu ati,
  • Hymn 475 Mbuye ndikhaletu
  • Hymn 148 PAKUPEMPHA ife pano,
  • Hymn 215 Choka, choka,
  • Hymn 1796 Ndikhulupira mwa Ambuye
  • Hymn 38 ANGELO ayimba,
  • Hymn 698 Polenga dzikoli,
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 417 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 443 M’MAŴA tizifesa
  • Hymn 471 YESU Mbuye ’Nu wofatsa
  • Hymn 187 UFUNA kuwomboledwa kodi?
  • Hymn 362 Imvani Yesu akuti:
  • Hymn 1025 Ndikamayenda m’mdimamo,
  • Hymn 1071 Kumwamba Yesu mthandize,
  • Hymn 449 MLENGI wathu Woyeranu,
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 492 Yesu Mbuye ‘Nu wafatsa
  • Hymn 359 TADZUKA mzimu wanga ‘we,
  • Hymn 694 Sadalekeza kuyamika
  • Hymn 1624 Koma anthu onse omwe
  • Hymn 652 Munene Mbuye ‘nenetu,
  • Hymn 1745 Yesu aitana ife:
  • Hymn 1003 Kanganani nkhondo yanu
  • Hymn 711 Ife tonse tichenjere
  • Hymn 781 Tatsegukani inutu,
  • Hymn 532 Ukondwere mtima wanga
  • Hymn 918 Ntchito yonse yakeyo
  • Hymn 1839 Yehova ndiye Mbusa wanga sin’ngasowe konse;
  • Hymn 1288 Yesu mundimve, ndikuliratu,
  • Hymn 137 UTHENGA wa Ambuye
  • Hymn 130 PHWANDO la Belisazara,
  • Hymn 226 Nditama mwaziwo!
  • Hymn 616 Dziko lathu lonseli
  • Hymn 78 ALINKUDZA wansoni Munthu,
  • Hymn 977 Musagonje, anthu inu,
  • Hymn 466 Yesu, muli pa chimpando
  • Hymn 1852 Mbuye ndamva mwawazira
  • Hymn 1567 Mubwere Mzimu Wakuyera,
  • Hymn 36 AMBUYE tsopano lino, monga mwa mawu anu aja,
  • Hymn 1761 Amithenga anaimba
  • Hymn 617 Nthawi yina Mbuyeyu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version