Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 964 Kodi simuona njira,

  1. Home   »  
  2. Hymn 964 Kodi simuona njira,

Hymn 964 Kodi simuona njira,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 964 Kodi simuona njira,

 

Kodi simuona njira,

Inu anthu akufoka?

Ayi, atiperekeza

Mbuye wathu wotikonda

Iye amakhala nafe,

Natitsogolera ife,

Atitsogolera ife

Kuli dzikolo labwino.

Atitsogolera ife

Kuli dzikolo labwino.

Post navigation

Previous: Hymn 963 Aulendo, munka kuti
Next: Hymn 965 Mundiuze, aulendo,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 305 NDALIMVA dziko la m’talimo,
  • Hymn 115 NTHAWI ija ya Sauli,
  • Hymn 736 Mndidyetse m’chipululu
  • Hymn 550 Wosauka Iyedi
  • Hymn 1110 Mulungu wanga,
  • Hymn 911 Mokhala mokhamokha
  • Hymn 1669 Ukafuna kumdziwitsa,
  • Hymn 240 YESU ndiye Mbuye wanga,
  • Hymn 888 Polowa ndi Inu
  • Hymn 147 MUSAŴALOLE mawuwo
  • Hymn 843 M’maiko monse, zisi zomwe,
  • Hymn 34 AMITHENGA a Mulungu,
  • Hymn 1 NDINU wakuyera! Wamphamvu zonse.
  • Hymn 651 Ikhale ngati nyali
  • Hymn 26 NDIKULEMEKEZA
  • Hymn 150 MIPINGO iyo idzatu,
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 810 Tsopano lino kwada bii,
  • Hymn 260 ODALA ndi onsewo,
  • Hymn 99 Tsopano ndimwona Iye
  • Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu,
  • Hymn 95 Palibe mmodzi akanatha
  • Hymn 709 Munthu aganize
  • Hymn 1106 Mlungu ndi wachikhalire.
  • Hymn 1294 Wakuba uja nachiona,
  • Hymn 415 Tidzalandirabe komwe
  • Hymn 976 Muyendenso kunka komwe,
  • Hymn 731 Mundionetse, Yesu,
  • Hymn 92 Ufuna kugwira ntchito yake?
  • Hymn 1464 Nditama Nsembe ya Mulungu,
  • Hymn 120 MUNDINYEMERE ’ne
  • Hymn 37 YESU analikhanda
  • Hymn 869 Anatipatsa Mawu onse olimbitsa mtima;
  • Hymn 444 YEMWE afesa nalira,
  • Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe
  • Hymn 1431 Lero lino m’bale wanga,
  • Hymn 918 Ntchito yonse yakeyo
  • Hymn 231 Mwazi wa Yesu wokondwa
  • Hymn 1019 Tsata, tsata, nditsatadi Yesu;
  • Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,
  • Hymn 862 Tidza kwa Mulungu Inu, ndinu wa chifundo;
  • Hymn 1166 Masauko athu
  • Hymn 571 Kwa ife lero anabadwa
  • Hymn 221 Yesu and’itana,
  • Hymn 138 SANGALATSA akusowa, masiku alikutha,
  • Hymn 364 Ali wokhululukira;
  • Hymn 1787 Mulungu wanga ndiye wachifundo
  • Hymn 529 Zili nazotu nkhwimba zirombozo,
  • Hymn 394 Titanka kwathu mkhale nafeko,
  • Hymn 893 Mtima wanga ndikonzera,
  • Hymn 391 Mufafanize m’bukumo
  • Hymn 1437 Yesu ndi wokonda;
  • Hymn 112 Pangano lake m’mwaziwo
  • Hymn 922 Onse akulapawo
  • Hymn 243 KONDWANI nonsenu,
  • Hymn 1028 Yendani bwino m’njiramo
  • Hymn 1676 Kondwerani dzuwa lino Aleluya,
  • Hymn 1602 M’mawu a Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 199 Watitsogolera Mbuye,
  • Hymn 405 M’mtima mwangamu mlowemo,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version