Hymn 562 Mwa ubwana wake wonse December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 562 Mwa ubwana wake wonse Mwa ubwana wake wonse Anakula m’mtima phee! Anakonda, anafatsa, Amay’ wake namvabe; Ndipo ana nonsenu, Mukamtsate bwinotu.