Hymn 562 Mwa ubwana wake wonse treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 562 Mwa ubwana wake wonse Mwa ubwana wake wonse Anakula m’mtima phee! Anakonda, anafatsa, Amay’ wake namvabe; Ndipo ana nonsenu, Mukamtsate bwinotu.