Hymn 525 Afike masiku December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 525 Afike masiku Afike masiku akuti anthu onse Adzamva mawu anu ndi kutsata inu nokha; Muwale mtima mwawomo, Adziwe muwakondanso; Kopani anthu abwere kwa Inu, Kopani anthu abwere kwa Inu.